Mt. 6:9-10
Mt. 6:9-10 BLY-DC
Nchifukwa chake popemphera muziti, “Atate athu akumwamba, dzina lanu lilemekezedwe. Ufumu wanu udze. Kufuna kwanu kuchitidwe, monga kumwamba chomwechonso pansi pano.