1
Yohana 15:5
Nyanja
NTNYBL2025
“Ine ni mzabibu, anyiimwe ni ndhawi. Yao akhala mkati mwanga, nane nikakhala mkati mwao, achameneo sachite vindhu vabwino vambili, popande ine simukhoza kuchita kandhu.
ប្រៀបធៀប
រុករក Yohana 15:5
2
Yohana 15:4
Khalani mkati mwanga, ngati umo ine nikhalila mkati mwanu. Ngati umo ndhawi ya mzabibibu siikhoza kubala yokha vipacho popande kukhala mumtengo wa mzabibu, chimwecho anyiimwe simukhoza kuchita chijha achifuna Amnungu ngati simukhala mkati mwanga.”
រុករក Yohana 15:4
3
Yohana 15:7
Anyiimwe mkakhala mkati mwanga ni mawu yanga yakakhala mkati mwanu, chipano, pembhani chilichonjhe icho mfuna namwe simpachidwe.
រុករក Yohana 15:7
4
Yohana 15:16
Anyiimwe simudanisanghe ine, nambho ine nidakusanghani anyiimwe nakutumani mkachite ivo avifuna Amnungu, ni njhito azifuna Amnungu izo sizikhaliche siku zonjhe.
រុករក Yohana 15:16
5
Yohana 15:13
Palibe chikondi chachikulu kupunda kusiyana ni chikondi cha mundhu uyo wachocha umoyo wake ndande ya bwenji lake.
រុករក Yohana 15:13
6
Yohana 15:2
Ndhawi yaliyonjhe iyo siibala vipacho mkati mwanga, Atate aidula, ni ndhawi iyo ibala aikonjezela ijhipunda kubala.
រុករក Yohana 15:2
7
Yohana 15:12
Lamulo langa nde ili, mkondane ngati ine umo nidakukondelani anyiimwe.
រុករក Yohana 15:12
8
Yohana 15:8
Atate wanga apachidwa ulemelelo yapo mchita vindhu ivo vakwadilicha Amnungu, namwe simukhale oyaluzidwa wanga.
រុករក Yohana 15:8
9
Yohana 15:1
Ndiipo Yesu wadakamba, “Ine ni mzabibu wa zene, ni Atate nde amlimi.
រុករក Yohana 15:1
10
Yohana 15:6
Mundhu wakasiya kukhala mkati mwanga wataidwa kubwalo ngati ndhawi ni kuuma. Ndhawi ngati zimenezo wandhu azikusa ni kuzitaya pamoto zipyelele.
រុករក Yohana 15:6
11
Yohana 15:11
“Nakukambilani vindhu ivi dala chimwemwe changa chikale mkati mwanu, ni chimwemwe chanu chikwanile.
រុករក Yohana 15:11
12
Yohana 15:10
Mkachita ngati umo afunila Atate ni kukhala muchikondi changa, ngati ine umo nichitila umo afunila Atate wanga ni kukhala mu chikondi chao.”
រុករក Yohana 15:10
13
Yohana 15:17
Chipano, lamulo langa kwanu nde ili, kondanani anyiimwe kwa anyiimwe.”
រុករក Yohana 15:17
14
Yohana 15:19
Ngati mudakali wandhu ajhiko, jhiko lidakakukondani ngati wandhu wake. Pakuti anyiimwe osati ajhiko, nambho ine nakusanghani kuchoka mujhiko, ndendande wandhu ajhiko akuipilani.
រុករក Yohana 15:19
គេហ៍
ព្រះគម្ពីរ
គម្រោងអាន
វីដេអូ