Chipano anyiimwe muli ni chisoni, nambho ine sinikujeleninjhoni, ni mitima yanu siikondwe, ni palibe mundhu uyo siwachichoche chimwemwe kwanu.”
“Siku limenelo simunipembha ine chilichonjhe. Zene nikukambilani, chilichonjhe icho simwaapembhe Atate ngati umo nifunila saakupacheni.