1
Yohana 14:27
Nyanja
NTNYBL2025
“Mtendele nikusiilani, nikupachani mtendele wanga. Yetu nikupachani osati ngati umo likupachilani jhiko la panjhi. Simudakhaikila mumtima ni simdaopa.
ប្រៀបធៀប
រុករក Yohana 14:27
2
Yohana 14:6
Ndiipo Yesu wadamuyangha, “Ine namwene nde njila, naakambila wandhu uzene ni kwapacha umoyo wa muyaya. Palibe uyo wakhoza kupita kwa Atate ila kwanjila yanga.
រុករក Yohana 14:6
3
Yohana 14:1
Yesu waadakambila, “Simudadandaula mumitima yanu. Mwaakhulupilila Amnungu, munikhulupilile ni ine.
រុករក Yohana 14:1
4
Yohana 14:26
nambho Othandiza, Mzimu woyela, uyo samtume kukhala mmalo mwanga, siwakuyaluzeni kila kandhu ni kukukumbuchani yonjhe yayo nakukambilani.”
រុករក Yohana 14:26
5
Yohana 14:21
“Uyo wayalandila malamulo yanga ni kuyagwila, mmeneyo nde uyo wanikonda. Uyo wanikonda ine siwakondedwe ni Atate wanga, nane sinimkonde ni kujhijhiwicha kwa iye.”
រុករក Yohana 14:21
6
Yohana 14:16-17
Sinaapembhe Atate nawo sakupacheni Wakukuthandizani mwina, uyo siwakhale namwe muyaya. Iye ni Mzimu wa zene. Jhiko lapanjhi silikhoza kumlandila ndande silimuona kapina kumjhiwa. Nambho anyiimwe mumjhiwa ndande wakhala namwe ni wali mkati mwanu.”
រុករក Yohana 14:16-17
7
Yohana 14:13-14
Chilichonjhe icho simupembhe ngati umo nifunila sinichite, dala Atate apachidwe ulemelelo mkati mwa Mwana. Mkanipembha chilichonjhe ngati umo nifunila, sinikuchitileni.”
រុករក Yohana 14:13-14
8
Yohana 14:15
“Ngati mnikonda malamulo yanga yawo nikupachani simuya chitile njhito.
រុករក Yohana 14:15
9
Yohana 14:2
Munyumba ya Atate wanga muli ni makhalo yambili, ngati siidakali chimwecho, nidakakukambilani. Chipano nipita kukukonjelani malo.
រុករក Yohana 14:2
10
Yohana 14:3
Nikapita kukukonjelani malo, sinibwele kukutengani mujhe kwanga, yapo nili ine namwe mukhalepo.
រុករក Yohana 14:3
11
Yohana 14:5
Tomaso wadamfunjha, “Ambuye, uko mpita ife sitikujhiwa, sitiijhiwe bwanji njila yopita kumeneko?”
រុករក Yohana 14:5
គេហ៍
ព្រះគម្ពីរ
គម្រោងអាន
វីដេអូ