1
Mk. 3:35
Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa
BLY-DC
Aliyense wochita zimene Mulungu akufuna, ameneyo ndiye mbale wanga ndi mlongo wanga ndi amai anga.”
مقایسه
Mk. 3:35 را جستجو کنید
2
Mk. 3:28-29
“Ndithu ndikunenetsa kuti anthu angathe kukhululukidwa machimo onse, ngakhalenso zonena zao zonse zomunyoza Mulunguyo. Koma aliyense wonyoza Mzimu Woyera, sadzakhululukidwa konse. Tchimo lakelo limakhala mpaka muyaya.”
Mk. 3:28-29 را جستجو کنید
3
Mk. 3:24-25
Anthu a mu ufumu uliwonse akayamba kuukirana, ufumuwo sungalimbe. Ndipo anthu a m'banja limodzi akayamba kugaŵikana, banja lotere silingalimbe.
Mk. 3:24-25 را جستجو کنید
4
Mk. 3:11
Mizimu yoipa inkati ikamuwona, inkadzigwetsa pansi pafupi ndi Iye nkumafuula kuti, “Inu ndinu Mwana wa Mulungu.”
Mk. 3:11 را جستجو کنید