Nanunso tsono khalani maso, chifukwa simudziŵa mwini nyumba adzabwerera nthaŵi yanji: kaya ndi madzulo, kaya ndi pakati pa usiku, kaya ndi tambala woyamba, kapena mbandakucha. Atha kudzabwera mwadzidzidzi, tsono asadzakupezeni muli m'tulo. Zimene ndikunenazi, sindikuuza inu nokha ai, koma ndikuuza anthu onse kuti, ‘Khalani maso.’ ”