1
Miyambo 26:4-5
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
CCL
Usayankhe chitsiru monga mwa uchitsiru wake, kuopa kuti ungadzakhale ngati chitsirucho. Koma nthawi zina umuyankhe monga mwa uchitsiru wake, kuopa kuti angamadziyese yekha wanzeru.
Compare
Explore Miyambo 26:4-5
2
Miyambo 26:11
Chitsiru chimene chimabwerezabwereza uchitsiru wake chili ngati galu amene amabwerera ku masanzi ake.
Explore Miyambo 26:11
3
Miyambo 26:20
Pakasowa nkhuni, moto umazima; chomwechonso pakasowa anthu amiseche mkangano umatha.
Explore Miyambo 26:20
4
Miyambo 26:27
Ngati munthu akumba dzenje, adzagweramo yekha; ngati munthu agubuduza mwala, udzamupsinja iye mwini.
Explore Miyambo 26:27
5
Miyambo 26:12
Munthu wa uchitsiru aliko bwino popeza pali chiyembekezo kuposana ndi munthu amene amadziyesa yekha kuti ndi wanzeru.
Explore Miyambo 26:12
6
Miyambo 26:17
Munthu wongolowera mikangano imene si yake ali ngati munthu wogwira makutu a galu wongodziyendera.
Explore Miyambo 26:17