1
Miyambo 27:17
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
CCL
Chitsulo chimanoledwa ndi chitsulo chinzake, chomwechonso munthu amanoledwa ndi munthu mnzake.
Compare
Explore Miyambo 27:17
2
Miyambo 27:1
Usamanyadire za mawa, pakuti sudziwa zimene zidzachitike pa tsikulo.
Explore Miyambo 27:1
3
Miyambo 27:6
Munthu amene amakukonda ngakhale akupweteke zili bwino, koma mdani wako amakupsompsona mwachinyengo.
Explore Miyambo 27:6
4
Miyambo 27:19
Monga momwe nkhope imaonekera mʼmadzi, chomwechonso mtima wa munthu umadziwika ndi ntchito zake.
Explore Miyambo 27:19
5
Miyambo 27:2
Munthu wina akutamande, koma osati wekha; mlendo akakutamanda, ndiponi koma osati ndi pakamwa pako.
Explore Miyambo 27:2
6
Miyambo 27:5
Kudzudzula munthu poyera nʼkwabwino kuposa chikondi chobisika.
Explore Miyambo 27:5
7
Miyambo 27:15
Mkazi wolongolola ali ngati mvula yamvumbi.
Explore Miyambo 27:15