Alom 6:17-18
Alom 6:17-18 NTNYBL2025
Nambho chipano nimuyamika Mnungu, pakuti anyiimwe kale mdali akapolo amachimo, mwakhala ovela kwa mtima yanu yonjhe kwa mayaluzo mdayaluzidwa. Mdaomboledwa kuchokela kuukapolo wa machimo, chipano mwakhala akapolo akuchita yajha yamkwadilicha Mnungu.


