Alom 1:17

Alom 1:17 NTNYBL2025

Pakuti uthenga wa bwino walangiza umo Mnungu wafunila tikhale kuti tivomelezeke pachogolo pake, chindhu ichi chichitika kwa kumkhulupilila Yesu Kilisito, palibe china kupitilila chimecho, ngati umo yalembedwa mmalembo, “Mundhu wovomelezeka kwa Mnungu siwakhale kwa kumkhulupilila Mnungu.”

អាន Alom 1