Luka 24:2-3

Luka 24:2-3 NTNYBL2025

Yapo adafika kumanda, adakomana mwala ujha waukulu lagunghulichidwa kutali ni pakhomo chiliza. Nambho yapo adalowa mkati mwa chiliza, sadalipheze chitanda la Ambuye Yesu.

អាន Luka 24