Luka 18

18
Chifani cha wamkazi wafedwa ni mmunake ni mlamuli wa milandu
1Ndiipo Yesu wadaakambila ochatila chifani ichi kwaalangiza umo afunikila kupembhela popande kulema. 2Wadakamba, “Mmujhi umojhi padali mlamuli wa milandu mmojhi uyo siwamamuope Mnungu kapina kusamala mundhu. 3Mmujhi umeneo padali maye mmojhi uyo wadafedwa ni mmunake, uyo wamajha kwaiye kila mala kumpembha kupunda, ‘Chonde munithangatile kuti nipate chuma changa kuchoka kwa mdani wanga.’ 4Pasiku zambili mlamuli wa milandu yujha siwamafune kumthangatila maye yujha wafedwa ni mmunake. Nambho pothela wadajhikambila mumtima, ‘Ingakhale kuti ine sinimuopa Mnungu kapina kusamala mundhu, 5nambho pakuti uyu wamkazi wafedwa ni mmunake wanichaucha kupunda, sinimthangatile, nikasiya kumthangatila siwayendekele kunichaucha kwakujha kwanga tetete!’”
6Ndiipo, Ambuye adakamba, “Muyaganizile kupunda yayo wadayakamba mlamuli wa milandu uyo siwachita njhito yake umo ifunikila. 7Bwanji, Mnungu siwaathangatila wandhu wasangha yawo ampembha kupunda popande kulema usana ni usiku? Bwanji, siwachedwa kwaapacha? 8Nikukambilani, kuti siwakupacheni yayo mfuna kwa chisanga. Bwanji, yapo siwafike ine mwana wa mundhu, bwanji sinapheze wandhu ali ni chikkulupi pano pajhiko?”
Chifani cha Mfalisayo ni wolandila malipilo
9Ndiipo Yesu wadakambila kwa chifani, wandhu anyiwajha amajhiona kuti avomelezeka pamaso pa Mnungu ni kwadelela wina, wadakamba, 10“Wandhu awili adapita ku nyumba ya Mnungu kukapembhela. Mmojhi wadali Mfalisayo ni mwina wadali wolandila malipilo. 11Yujha Mfalisayoyo wadaima ni kupembhela wadakamba kuusu iye mwene wake, ‘A Mnungu, nikuyamikani pakuti ine sinili ngati wandhu wina, anghunghu wina oyipa ni wina achigololo ni sinilingana ni mundhu ngati uyu wolandila malipilo. 12Nimanga kudya kawili pa jhuma, nichocha fungu limojhi pa kila mafungu khumi pa chuma changa icho nipata.’ 13Nambho wolandila malipilo yujha wadaima patali popande kukweza maso yake kumwamba, nambho wadajhibula pachidale kwa chisoni niwakamba, ‘Ambuye, nilengeleni lisungu ine wochimwa.’ 14Nikukambilani yujha wolandila malipilo wadabwelela kukhomo kwake wavomelezedwa pamaso pa Mnungu, kupitilila yujha Mfalisayo. Pakuti, waliyonjhe uyo wajhikweza siwachichidwe, ni waliyonjhe uyo wajichicha siwakwezedwe.”
Yesu waapacha mwawi wana wang'onoang'ono
Matayo 19:13-15; Maluko 10:13-16
15Wandhu wina amampelekela Yesu wana wang'onoang'ono wasanjike manja kuti waapache mwawi. Nambho oyaluzidwa wake yapo adaona chimwecho, wadaanyindila. 16Nambho Yesu wadaatana wana waang'ono niwakamba, “Alekeni wana waang'onowa ajhe kwaine, msadaachekeleza, pakuti Ufumu wa Mnungu ni wa wandhu ngati wawanawo. 17Nikukambilani uzene, mundhu waliyonjhe uyo siwaulandila Ufumu wa Mnungu ngati waanawa, siwalowelatu mu Ufumu wa Mnungu.”
Mchogoleli wopata
Matayo 19:16-30; Maluko 10:17-31
18Mchogoleli mmojhi wa Ayahudi wadamfunjha Yesu, “Oyaluza wabwino, nichite bwanji kuti nikalowe mu ufumu wa muyaya?”
19Yesu wadamuyangha, “Ndande yanji unitana oyaluza wabwino? Palibe uyo wali wabwino nambho Mnungu yokha. 20Malamulo uyajhiwa, ‘Usadachita chigololo, usadapha, usadaba, usadachocha umboni wamthila, lemekeza atate wako ni amako.’”
21Mchogoleli yujha wopata wadakamba, “Vonjhevo navichita kuyambila kuunyamata wanga.” 22Yesu yapo wadavela chimwecho, wadamkambila, “Nambho wachepekela chindhu chimmojhi, Gulicha kila kandhu yako ulinako, ni ndalamazo waagawile wosauka, ni iwe siuikile chuma chako kumwamba. Alafu majha, unichate.” 23Nambho mundhu mmeneyo yapo wadavela chimwecho wadali ni chisoni kupunda mumtima mwake, ndande wadali mundhu wa chuma chochuluka kupunda.
24Yesu wadampenya, wadakamba, “Penyani umo ilimbila kwa mundhu wopata kuwola mu Ufumu wa Mnungu! 25Yetu, ikhozekana kwa chinyama chitanidwa ngamila kupita pandhoolo ya singano kusiyana ni mundhu wopata kulowa mu Ufumu wa Mnungu.”
26Wandhu adavela yameneyo, adafunjhana, “Chipano, yani uyo siwakhoze kuomboka?”
27Yesu wadayangha, “Yayo siyakhozekana kwa mundhu, yakhozekana kwa Mnungu.”
28Ndiipo Petulo wadamuyangha Yesu, “Ife tasiya vindhu vatu vonhje ni kulamula kukuchata iwe!” 29Yesu wadaayangha, “Zenedi nikukambilani, palibe mundhu waliyonjhe uyo wasiya nyumba yake kapina wamkazake kapina mbale kapina wobala, kapina wana ndande ya Ufumu wa Mnungu, 30uyo siwalandila vochuluka kupunda nyengo ino ni nyengo ikujha ni kulandila umoyo wamuyaya.”
Yesu walosa mala ya katatu kuusu nyifa ni kupachikidwa kwake
Matayo 20:17-19; Maluko 10:32-34
31Yesu wadaatana kumbhepete woyaluzidwa wake khumi ni awili wajha, ni kwaakambila, “Vechelani! Tikwela kupita ku Yelusalemu ni kumeneko kila kandhu yako kalembedwa ni alosi kuusu Mwana wa Mundhu, sichikwanilichidwe. 32Mwana wa Mundhu siwapelekedwe mmanja mwa wandhu yawo samjhiwa Mnungu, samdelele, ni kumtukwana, ni kumlavulila malovu. 33Siabule mikwapulo ni kumpha, nambho siku la katatu siwahyuke.” 34Nambho woyaluzidwa wake sadave mate ya mawu yajha wamakamba Yesu, ndande yadabisidwa kwa anyiiwo ni siamajhiwe kuti Yesu wamakambilila chiyani.
Yesu wamulamicha mundhu wosapenya
Matayo 20:29-34; Maluko 10:46-52
35Yapo Yesu wadali pafupi kufika ku Yeliko, wadakomana ni mundhu mmojhi wosapenya, uyo wadakhala mbhepete mwanjila kupembhapembha. 36Yapo wadavela wandhu ambili niapita, wadafunjha, “Kuli chiyani?” 37Adamuyangha, “Yesu wa ku Nazaleti watopita.” 38Ndiipo wosapenya mmeneyo wadakweza mvekelo, wadakamba, “Yesu Mwana wa Daudi, unilengele lisungu!” 39Anyiwajha adali mchogolo adamnyindila kuti wakhale chete. Nambho iye wadaendekela kukweza mvekelo waukulu, “Mwana wa Daudi chonde, unilengele lisungu!” 40Yesu wadaima ni kwalamula kuti ajhenayo kwaiye. Wosapenya yujha yapo wadafika pafupi, Yesu wadafumnjha, 41“Ufuna nikuchitile chiyani?” Iye wadayangha, “Ambuye nifuna nikhoze kupenya.” 42Yesu wadamuyangha, “Penya, chikhulupililo chako chakulamicha.” 43Pampajha mundhu yujha wadakhoza kupenya, wadamchata Yesu uku niwamkweza Mnungu. Yapo adaona chimwecho, wandhu wonjhe adamtamanda Mnungu.

ទើបបានជ្រើសរើសហើយ៖

Luka 18: NTNYBL2025

គំនូស​ចំណាំ

ចែក​រំលែក

ចម្លង

None

ចង់ឱ្យគំនូសពណ៌ដែលបានរក្សាទុករបស់អ្នក មាននៅលើគ្រប់ឧបករណ៍ទាំងអស់មែនទេ? ចុះឈ្មោះប្រើ ឬចុះឈ្មោះចូល