Yohana 2
2
Ukwati mmujhi wa Kana
1Siku la katatu kudali ni ukwati mmujhi wa Kana, mkoa wa ku Galilaya, nawo amaye wake Yesu adalipo pamwepo, 2Yesu naye wadalalikidwa pa ukwati pamojhi ni oyaluzidwa wake. 3Divai yapo idatha, amaye wake adamkambila Yesu, “Divai yatha.”
4Ndiipo Yesu wadayangha amaye wake, “Ndandeyanji munikambila nghani imeneyo. Ndhawi yochita njhito yanga ikali yosafika.”
5Chimwecho amake adazikambila mbowa, “Chilichonjhe icho siwakukambileni, chitani,”
6Pamenepo padali ni mapipa sita ya myala, iyo yaikidwa kwa chikhalidwe chakusamba cha Chiyahudi, kila mchuko udakakhoza kutenga michuko ya wili kapina itatu ya majhi. 7Ndiipo Yesu wadaakambila, “Jhazani majhi mmapipa.” 8Ndiipo wadaakambilanjho, “Chipano tungani mkampelekele wamkulu wa phwando.” 9Wamkulu waphwando yapo wadalawa majhi yameneyo, wadapeza yang'anamuka kukhala divai. Siwada jhiwe uko ya choka, nambho anyiyawo adatunga majhi adajhiwa. Wamkulu wa phwando wadamtana wammuna wa ukwati, 10wadamkambila, “Kila mudhu wayamba kwapacha wandhu divai ya bwino uti, ni akathokumwa ni kukwana, wakonja ijha yosakome. Nambho iwe wachocha divai ya bwino mbaka saino.”
11Yesu wadachita chizindikilo ichi choyamba ku Kana, ya ku Galilaya wadaalangiza ulemelelo wake, ni oyaluzidwa wake adamkhulupilila.
12Pambuyo, Yesu wadachika pamojhi ni amaye wake ni achabale wake ni oyaluzidwa wake, adapita ku Kapelinaumu uko adakhala kwa masiku yochepa.
Yesu wapita ku Nyumba ya Amnungu
Matayo 21:12-13; Maluko 11:15-17; Luka 19:45-46
13Phwando la Pasaka la Ayahudi lidawandikila, chimwecho Yesu wadakwela kupita ku Yelusalemu. 14Ndiipo wadaapheza wandhu mujha mu Nyumba ya Amnungu niaghulicha ng'ombe, mbelele ni nghunda ni ong'anamula ndalama akhala pa gome. 15Wadakonja mkwapulo wa maluzi, nikwatopola onjhe apite kubwalo pamojhi ni ng'ombe ni mbelele zao, wadataya ndalama za anyiyao amang'anamula ndalama ni kuzigadabula gome zao. 16Wadakambila anyiwajha amaghulicha nghunda, “Chochani vindhu ivi pano. Simuda chita Nyumba ya Atate wanga kukhala pamalo pa malonda!” 17Oyaluzidwa wake adakumbukila malembo yayo yalembedwa chimwechi, “Chikondi changa mu Nyumba mwanu siuniphe.”
18Ayahudi akumojhi adamfunjha Yesu, “Ukhoza kuchita chizindikilo chanji kulangiza kuti iwe uli ni ulamuli wochita vindhu ivi?”
19Yesu wadaayangha, “Gomolani Nyumba ya Amnungu ino, nane siniimange kwa siku zitatu.”
20Ndiipo Ayahudi adamfunjha, “Nyumba ya Amnungu ino idamangidwakwa vyaka alubaini ni sita, bwanji iwe siukhoze kuimanga kwa siku zitatupe?”
21Nambho Nyumba ya Amnungu iyo Yesu waichula ni thupi lake. 22Yapo wadahyuchidwa, oyaluzidwa wake adakumbukila kuti wada kambapo chimwecho, ndipo adayakhulupilila malembo yoyela ni mawu yayo wadakamba Yesu.
Yesu waijhiwa mitima ya wandhu
23Yesu yapo wadali ku Yelusalemu ku phwando la Pasaka, wandhu ambili ada mkhulupilila yapo adaona vizindikilo ivo wadachita. 24Nambho Yesu siwadakhulupilile chikhulupi chao kwake, ndande onjhe wamaijhiwa mitima yao. 25Siwadafune kukambilidwa chili chonjhe kuusu wandhu, pakuti wadavijhiwa vindhu vonjhe ivo vili mmitima mwawo.
ទើបបានជ្រើសរើសហើយ៖
Yohana 2: NTNYBL2025
គំនូសចំណាំ
ចែករំលែក
ចម្លង

ចង់ឱ្យគំនូសពណ៌ដែលបានរក្សាទុករបស់អ្នក មាននៅលើគ្រប់ឧបករណ៍ទាំងអស់មែនទេ? ចុះឈ្មោះប្រើ ឬចុះឈ្មោះចូល
The New Testament in Nyanja @The Word for The World International and Nyanja Language translation, 2025. All rights reserved.

: