Yohana 18

18
Kugwilidwa kwa Yesu
Matayo 26:47-56; Maluko 14:43-50; Luka 22:47-53
1Yesu yapo wadamaliza kukamba, wadachoka ni oyaluzidwa wake kupita kuchija la mchinje Keduloni. Pamenepo yapo idavyalidwa mitengo ya Mizeituni, wadalowa mmenemo iye ni oyaluzidwa wake. 2Yuda, uyo wamafuna kumng'anamuka Yesu, wadapajhiwa pamalo pamenepo pakuti wamapita kumeneko mala zambili ni oyaluzidwa wake. 3Ndiipo, Yuda wadaatenga asikali ni alonda kuchokela kwa ajhukulu waakulu ni Afalisayo, wadajha nao kubusitani watenga nyali, myenje ni vida. 4Chimwecho Yesu yapo wadayajhiwa yonjhe yayo siyampheze, wadatulukila pachogholo pao, wadafunjha, “Mumfunafuna yani?”
5Ndiipo adamuyangha, “Yesu wakunazaleti!”
Yesu wadakambila, “Ine nde mwene.”
Yuda wadaima pamojhi nao. 6Chimwecho, Yesu yapo wadaakambila, “Ine nde mwene,” Adabwela kumbuyo, ni kughwa panjhi. 7Yesu wadaafunjhanjho, “Mumfunafuna yani?”
Adayangha, “Yesu wa ku Nazaleti!”
8Yesu wadaakambila, “Natho kukambilani kuti ine nde mwene. Chimwecho, ngati munifunafuna ine, asiyeni anyiyawa ajhipita.” 9Wadakamba yameneyo dala yakwanile mawu yayo wadakamba, “Anyiyao mudanipacha palibe uyo namsoweza.”
10Simoni uyo Yesu wadamtana Petulo wadali ni mpeni, wadausolola, wadamdula khutu la kwene mbowa wa mjhukulu wamkulu. Mbowa mmeneyo wamatanidwa Maluko. 11Ndiipo, Yesu wadamkambila Petulo, “Bweza mpeni wako mthumba lake. Bwanji, sinida vutika mavuto yayo anipacha Atate?”
Yesu wapelekedwa kwa mjhukulu wamkulu
12Ndiipo ghulu la asikali, ni wamkulu wa asikali Aloma ni alonda a Mnyumba ya Amnungu adamgwila Yesu, ni kummanga maluzi, 13ni kumpeleka huti kwa Anasi, mpongozi wa Kayafa, uyo wadali mjhukulu wamkulu chaka chimenecho. 14Kayafa mmeneyo nde uyo wadapacha mwambo Ayahudi kuti mbasa wafe mmojhi ndande ya wandhu ambili.
Petulo wamkana Yesu
Matayo 26:69-70; Maluko 14:66-68; Luka 22:55-57
15Simoni Petulo ni oyaluzidwa mwina uyo wamamchata Yesu. Oyaluzidwa mwinayo wamajhiwika ni mjhukulu wamkulu, chimwecho wadalowa pamojhi ni Yesu mkati mwa khumbi la mjhukulu wamkulu. 16Nambho Petulo wadaima kubwalo pafupi ni chicheko. Chimwecho oyaluzidwa mwinayo uyo wamajhiwika ni mjhukulu wamkulu wadatuluka kubwalo kupita kukambana ni mwali uyo wamalonda pachicheko, Petulo walowe mkati. 17Mbowa yujha, wamalonda pa chicheko wadamfunjha Petulo, “Bwanji, iwe mmojhi wa oyaluzidwa amundhu uyu?”
Petulo wadayangha, “Asati ine!”
18Chimwecho mbowa ni alonda amaotha moto ndande kudali ni mbhepo. Ni Petulo nayo wadaima nao pamwepo kuotha moto.
Mjhukulu wamkulu wamfunjha Yesu
Matayo 26:59-66; Maluko 14:55-64; Luka 22:66-71
19Ndiipo mjhukulu wamkulu wadamfunjha Yesu nghani za oyaluzidwa wake ni mayaluzo yake. 20Yesu wadamuyangha, “Nakamba ni wandhu padanga. Nyengo zambili nimayaluza munyumba za zokomanilana za Ayahudi ni mnyumba ya Mnungu, pamalo yapo aphezana Ayahudi onjhe, sinidakambe kandhu kobisa. 21Ndande yanji unifunjha ine? Afujhe anyiyao avela icho nakambila. Anyiwo ajhiwa yayo nakambila.”
22Yapo waadakamba yameneyo mlonda mmojhi uyo wadaima pafupi nayo wadaombela mmanja waadakamba, “Bwanji umuyangha chimwechi mjhukulu wamkulu?”
23Yesu wadaadayangha, “Ngati nakamba kuipa, nilangize kuipako, ngati nakamba bwino, mbona unibula?”
24Ndiipo Anasi wadampeleka Yesu waliomangidwa, kwa Mjhukulu Mamkulu wa Kayafa.
Petulo wamkananjho Yesu
Matayo 26:71-75; Maluko 14:69-72; Luka 22:58-62
25Petulo wamaotha moto. Adamfunjha, “Iwe uli mmojhi wa oyaluzidwa wake?”
Nambho Petulo wadakana ni kukamba, “Osati ine.”
26Mbowa mmojhi wa mjhukulu wamkulu, mbale wa mundhu yujha wadadulidwa kuthu ni Petulo, adamfunjha, “Ine nidakuona pamojhi naye ku busitani”
27Petulo wadakananjho, posachedwe tambala wadalila.
Yesu pachogholo pa Pilato
Matayo 27:1-2,11-14; Maluko 15:1-5; Luka 23:1-5
28Ndiipo adamtenga Yesu kuchokela kwa Kayafa, adampeleka kuikulu. Idali mmalenga kucha, nambho anyiiwo sadalowe muikulumo, dala sadakhala najisi, akhoze kudya pasaka. 29Chimwecho, wadaachota kubwalo, wadakamba, “Kuli loipa liti kwa mundhu uyu?”
30Adamuyangha, “Ngati siwadakali oyipa mundhu uyu sitidaka mpeleka kwanu.”
31Ndiipo Pilato wadakambila, “Chipano mtengeni mwachinawene, mumlamule kuchokana ni thauko lanu.”
Ayahudi adayangha, “Ife tilibe lamulo la kupha mundhu waliyonjhe.” 32Idachitika chimwecho dala yakwanile mawu yayo wadakamba Yesu kulangiza nyifa yanji iyo siwafe.
33Ndiipo Pilato wadalowanjho mnyumba yake ya chifumu, ni kuagiza Yesu wapelekedwe wadamfunjha, “Bwanji iwe nde Mfumu wa Ayahudi?”
34Yesu wadamuyangha, “Yameneyo maganizo yako kapina akukambila wandhu nghani zanga?” 35Ndiipo Pilato wadayangha, “Bwanji ine Myahudi? Jhiko lako ni ajhukulu akupeleka kwanga. Walakwa chiyani?”
36Ndiipo Yesu wadayangha, “Ufumu wanga asati wajhiko lino. Ngati Ufumu wanga udakali wajhiko lino, ochatila wanga adakani menyela nghondo sinidagwilidwa ni Ayahudi. Nambho ufumu wanga asati wa jhiko lino.”
37Chimwecho Pilato wadamkambila, “Chipano iwe Mfumu?” Yesu wadayangha, “Iwe umo wakambila kuti ine Mfumu. Ine nabadwa dala nikhale mfumu, kwa ndande imeneyo najha pajhiko kwakambila wandhu uzene. Kila mundhu wazene wavela mvekelo wanga.”
38Pilato wadamkambila, “Zene nde chiyani?”
Yesu walamulidwa kufa
Matayo 27:15-31; Maluko 15:6-20; Luka 23:13-25
Pilato yapo wadakamba yameneyo, wadachotanjho Ayahudi kubwalo, wadakambila, “Ine sinidachione chilichonjhe icho walakwa mundhu uyu. 39Nambho kwanu kuli ni chikhalidwe kuti ndhawi ya Pasaka nimmasulile omangidwa mmojhi. Chipano mfuna nimmasulile Mfumu wa Ayahudi?”
40Ndiipo adabula mapokoso, “Notho! Asati uyu nambho timasulileni Balaba!” Nayo balaba wadali olanda. Wadali ni alonda kuchokela kwa ajhukulu waakulu ni Afalisayo, wadajha nao kubusitani watenga nyali, myenje ni silaha.

ទើបបានជ្រើសរើសហើយ៖

Yohana 18: NTNYBL2025

គំនូស​ចំណាំ

ចែក​រំលែក

ចម្លង

None

ចង់ឱ្យគំនូសពណ៌ដែលបានរក្សាទុករបស់អ្នក មាននៅលើគ្រប់ឧបករណ៍ទាំងអស់មែនទេ? ចុះឈ្មោះប្រើ ឬចុះឈ្មោះចូល