Yohana 16
16
1“Nakukambilani yameneyo dala nikuimicheni nganganga kuti simudachisia chikhulupillilo chanu. 2Wandhu sakutopoleni munyumba zao zokomanilana Ayahudi ni kulambila. Ndhawi ikujha waliyonjhe uyo wakuiphani anyiimwe siwaghanizile kuti wamtumikila Amnungu. 3Sakuchitileni vindhu vimenevo ndande saajhiwa Atate, ni sanijhiwa ine. 4Basi, nakukambilani vindhu ivi dala ndhawi ikajha, mkumbukile kuti nidathokukambilani.
Njhito ya Mzimu Oyela
“Sinidakukambileni vindhu ivi kuyambila mmayambo ndande nidali pamojhi namwe. 5Chipano nipita kwayao anituma, nambho palibe uyo wanifunjha uko nipita. 6Pakuti nakukambilani vindhu vimenevo, mwajhalidwa ni chisoni mmitima mwanu. 7Nambho nikukambilani uzene, mbasa ine nipite, mate yake nikasiya kupita Othandiza siwajha kwanu. Nambho nikapita, sinimtume kwanu. 8Nayo yapo siwajhe siwachimikizile wandhu ajhiko nghani za machimo, kuvomelezeka ni lamulo la Amnungu. 9Achita machimo, ndande sanikhulupilila, 10Mzimu woyela siwachimikizile kuusu kuvomelezeka kwanga pachogolo pa Amnungu, ndande nipita kwa Atate, nawo sanionanjho. 11Kuusu kulamula, ndande satana wamkulu wa jhiko lino, watho lamulidwa.
12“Nikali nayo yambili yakukukambilani, nambho kwa chipano simuyakhoza kuimila nganganga. 13Nambho yapo suujhe Mzimu wa uzene siukuchoghozeni kuuzene onjhe, iye siwakamba kwa lamulo lake mwene, nambho siwakambe yayo wayavela kuchoka kwanga ni kukujhiwichani vindhu ivo sivichokele pambuyo. 14Iye siwanipache ine ulemelelo pakuti siwakujhiwicheni yayo siwayapate kuchoka kwanga. 15Vonjhe alinavo Atate nivanga, ndendande nakamba kuti Mzimu wa uzene siukujhiwicheni ivo siwayapate kuchoka kwanga.”
Kukhala ni chisoni ni Chimwemwe
16“Ikali ndhawi yochepa, namwe simunionanjho, ni pambuyo pa ndhawi yochepa simunione!”
17Chimwecho oyaluzidwa wake wina adafunjhana, “Walinimate yanji yapo wakamba, ‘Ikali ndhawi yochepa simunionanjho, ni ndhawi yochepa simunionenjho?’ Ni wakambanjho, ‘Pakuti nipita kwa Atate!’ 18Wali ni mate yanji yapo wakamba, ‘Ikhali ndhawi yochepape?’ Sitijhiwa kuti wakamba chiyani.”
19Yesu wadajhiwa kuti amafuna kumfunjha, ndiipo wadaakambila, “Bwanji mfunjhana ndande nakamba, ‘Ikali ndhawi yochepa simuniona ni pambuyo pa ndhawi yochepa simunionenjho?’ 20Nikukambilani uzene, anyiimwe simulile ni kuchita zaya, nambho wandhu ajhiko sakondwe, simukhale ni chisoni nambho chisoni chanu siching'anamuke ni kukhala chimwemwe. 21Ndhawi iyo maye wajhimasula, wakhala ni chisoni ndande ndhawi yopweteka yafika, nambho wakatho jhimasula siwakumbukila kupweteka ndande ya chimwemwe chobadwa kwa mundhu pajhiko. 22Chipano anyiimwe muli ni chisoni, nambho ine sinikujeleninjhoni, ni mitima yanu siikondwe, ni palibe mundhu uyo siwachichoche chimwemwe kwanu.”
23“Siku limenelo simunipembha ine chilichonjhe. Zene nikukambilani, chilichonjhe icho simwaapembhe Atate ngati umo nifunila saakupacheni. 24Mbaka chipano simudanipembhe kandhu kalikonjhe kwa ulamulilo wanga. Pembhani namwe simupate dala chikondwelo chanu chikwanile.”
Yesu wazikhoza mbhavu zoipa za jhiko
25“Nikukambilani vindhu vimenevo kwa kukuluwika. Nambho ndhawi ikujha sinikamba namwe kwa kukuluwika, nambho sinikambe namwe padanga nghani za Atate. 26Siku limenelo simupembhe kuchokana ni anyiimwe umo munikhulupilila, ni sinikukambilani kuti sinikupembheleni kwa Atate, 27Pakuti Atate akukondani anyiimwe, ni ndande anyiimwe mwanikonda ine ni mwakhulupilila kuti nachoka kwa Amnungu. 28Ine nidachoka kwa Atate, nidajha pajhiko, ni chipano nilisiya jhiko nibwela kwa Atate.”
29Ndiipo, oyaluzidwa wake adamkambila, “Chipano ukamba popande kubisa ni siukamba kwa kukuluwika. 30Chipano tijhiwa kuti iwe ujhiwa kila kandhu, ni palibe ndande yakukufunjha mafunjho. Tikhulupilila kuti wachoka kwa Amnungu.”
31Yesu wadaafunjha, “Bwanji, mkhulupilila chipano? 32Ndhawi ikujha, ni yathofika yapo simmwazikane kila mmojhi siwapite kukhomo kwake, ni anyiimwe simunisiye ine nekha. Nambho ine sinilinekha, pakuti Atate alipamojhi niine. 33Nakukambilani vindhu ivi dala mukhale ni mtendele pakulunjana niine. Simvutike pajhiko, nambho jhipacheni mtima! Ine nazikhoza mbhavu zoipa za jhiko lino!”
ទើបបានជ្រើសរើសហើយ៖
Yohana 16: NTNYBL2025
គំនូសចំណាំ
ចែករំលែក
ចម្លង
ចង់ឱ្យគំនូសពណ៌ដែលបានរក្សាទុករបស់អ្នក មាននៅលើគ្រប់ឧបករណ៍ទាំងអស់មែនទេ? ចុះឈ្មោះប្រើ ឬចុះឈ្មោះចូល
The New Testament in Nyanja @The Word for The World International and Nyanja Language translation, 2025. All rights reserved.

: