Yohana 11
11
Kumwalila kwa Lazalo
1Padali ni mundhu mmojhi wa ku Besania, wamatanidwa Lazalo, wamadwala. Wamakhala kuchijhijhi cha Besania kumeneko amakhala ni achalongo wake Malia ni Masa. 2Malia uyu nde yujha wadaanyeka Ambuye mafuta ya mtengo wa ukulu yayo yanunghila ni kuichangula myendo kwa machichi yake. Mbale wake Lazalo nde uyo wadali odwala. 3Chimwecho achalongo wake Lazalo onjhe adatuma uthenga kwa Yesu, “Ambuye mmbwenji lanu wadwala!”
4Yesu yapo wadavela chimwecho, wadakamba, “Lazalo siwamwalila kwa utenda uno, nambho wadwala ndande ya kwaapacha Amnungu ulemelelo, wadwala dala Mwana wa Amnungu walemekezedwe kupitila utenda umeneo.”
5Yesu wadali ni ubwenji wa pamtima ni Masa ni Malia ni Lazalo. 6Yapo wadavela kuti Lazalo wadwala, Yesu wadaendekela kukhala pamalo pajha wadali kwa masiku yawili. 7Ndiipo pambuyo pa yameneyo, wadakambila oyaluzidwa wake, “Chipano tiyeni tibwelenjho ku Yudea!”
8Oyaluzidwa wake adamkambila, “Oyaluza! Yapita ndhawi yo chepa Ayahudi yapo amafuna kuiiphani kwa myala, ndande yanji mfuna kupitanjho kumeneko?”
9Yesu wadayangha, “Bwanji saa za usana osati khumi ni ziwili? Chimwecho mundhu akayenda usana siakhoza kujhikhuwala ndande aliona dangalila la jhiko lino. 10Nambho usiku mundhu wajhikwala ndande dangalila palibemo mkati mwake.” 11Yesu yapo wadakamba mawu yameneyo, wadaakambila, “Mbwenji lathu Lazalo waghona litulo, nambho ine sinipite kumuucha.”
12Oyaluzidwa wake adamkaambila, “Ambuye ngati waghona, siwauke.”
13Anyiiwo amaghaniza wamakamba kuti waghona litulo, nambho wamakambilila nyifa ya Lazalo. 14Ndiipo, Yesu wadakambila popande kwa bisa, “Lazalo wamwalila, 15nambho nikondwa ndande sinidalipo kumenepo yapo Lazalo wamamwalila. Chipano tiyeni kukhomo lake.”
16Tomaso uyo watanidwa mawila wadaakambila oyaluzidwa achanjake kuti, “Tiyeni nafe tikafe pamojhi ni Ambuye!”
Yesu nde uhyucho ni umoyo
17Yesu yapo wadajha kumeneko wadapheza chitanda cha Lazalo chatho khala siku zinayi mmainja. 18Kijhijhi cha Besania chidali pafupi ni Yelusalemu, utali wa kilometa zitatu kuchoka ku Yelusalemu. 19Ayahudi ambili adafika kwa masa ni Malia kwa tondeza kwa nyifa ya mlongo wao.
20Chimwecho Masa yapo wadavela kuti Yesu watokujha, wadapita kumlandila nambho Malia wadakhala pakhomo. 21Ndiipo Masa wadamkambila Yesu, “Ambuye, ngati mudakalipo pano, mlongo wanga siwadakafa! 22Nambho nijhiwa kuti atangati chipano chilichonjhe icho siwapembhe Amnungu, sakupacheni.”
23Ndiipo Yesu wadamkambila, “Mlongo wako siwahyuke.”
24Masa wadayangha, “Nijhiwa kuti siwahyuke ndhawi ya uhyucho, siku lo thela.”
25Yesu wadamkambila, “Ine nde uhyucho ni umoyo. Uyo wanikhulupilila ine atangati wakamwalila, siwakhale moyo, 26ni waliyonjhe uyo wakhala wa moyo ni khulupilila, siwamwalila muyaya. Bwanji ulikhulupilila ili?”
27Masa wadamkambila, “Etu Ambuye! Ine nikhulupila kuti imwe nde Kilisito uyo wasanghidwa ni Amnungu, Mwana wa Amnungu, uyo wakujha pajhiko.”
Yesu wamlilila Lazalo
28Pambuyo pa yameneyo, Masa wadapita kumtana Malia kwa chisisi, wadamkambila, “Oyaluza alipano, akutanani.” 29Nayo yapo wadavela chimwecho wadaima msangu, ni kumchata Yesu. 30Ni Yesu wadaliwakali osafike pa kijhijhi, wadali wakali pamalo pampajha wadalandilidwa ni Masa. 31Ndiipo Ayahudi anyiyawo adali mnyumba ni amtondeza Malia yapo adamuona mujha waima ni kutuluka kubwalo chisanga, adamchata. Amaghaniza wapita kumanda kuomboleza.
32Ndiipo, Malia yapo wadafika pamalo yapo wadali Yesu, wadagwada, wadamkambila, “Ambuye, ngati mudakali pano, mlongo wanga siwadakamwalila!”
33Yesu yapo wadamuona maliya walila, ni Ayahudi anyiyao adajha pamojhi ni Maliya nayo alila, wadali ni chisoni ni kudandaula mumtima. 34Ndiipo wadamfunjha, “Mwamzika kuti?”
Adamkambila, “Ambuye, majhani mpenye.”
35Yesu wadalila. 36Chimwecho, Ayahudi adakamba, “Penyani umo wamkondela Lazalo!”
37Nambho wina adakamba, “Uyu wadalamicha maso yujha sapenya, siwadakhoza kumlamicha Lazalo?”
Yesu wamuhyucha Lazalo
38Ndiipo Yesu uku ni wadandaula mumtima, wadafika yapo idali manda. Manda ene idali mbhanga, ni ida vinikilidwa mwala. 39Yesu wadakamba, “Uchocheni mwala!” Masa mlongo wake Lazalo, wadamkambila, “Ambuye, watho yamba kunungha, ndande wakhala mmanda siku zinai!”
40Yesu wadaamkambila Masa, “Bwanji sinidakukambileni kuti ukakhulupilila siuone ulemelelo wa Amnungu?” 41Ndiipo adauchocha ujha mwala. Yesu wadapenya kumwamba, wapemba, ni wakamba “Nikuyamikani Atate ndande mwanivela. 42Nijhiwa kuti munivela siku zonjhe. Nakamba yameneyo ndande ya wandhu alipano kuti apheze kukhulupilila kuti imwe nde yao mwanituma.” 43Yapo wadamaliza kukamba yameneyo, wadatana kwa mvekelo waukulu, “Lazalo, majha kuno kubwalo!” 44Yujha wadamwalila wadatuluka kubwalo, wali omangidwa sanda mmyendo ni mmanja, ni kumaso wavinikilidwa njhalu.
Yesu wadakambila, “Mmasuleni, mumsiye wajhipita.”
Achogoleli wa Ayahudi apanga kumpha Yesu
Matayo 26:1-5; Maluko 14:1-2; Luka 22:1-2
45Ndiipo, Ayahudi ambili anyiyao adafika ni Malia yapo adaona yayo wadachita Yesu, adamkhulupilila. 46Nambho wina wao adapita kwa Afalisayo kwaapacha nghani ya ivo wadachita Yesu. 47Chimwecho ajhukulu waakulu ni Afalisayo adachita msonghano wa bwalo la milandu lalikulu, adafunjhana, “Tichite bwanji? Mateyake mundhu uyu wachita vizindikilo vambili kupunda. 48Ngati tikamsiya waendekele kuchita vizindikilo ivi kila mmojhi siwamkhulupilile iye, ni achogoleli a Aloma saajhe kutichochela ulamulilo wathu wa Nyumba ya Amnungu ni jhiko lathu!”
49Mundhu mmojhi pakati pao uyo wamatanidwa Kayafa, uyo wadali mjhukulu wamkulu chaka chimenecho, wadaakambila, “Anyiimwe simujhiwa chindhu chilichonjhe! 50Simujhiwa kuti mbasa wafe mmojhi ndande ya wandhu, kusiyana liwanangidwe jhiko lonjhe?” 51Kayafa siwadakambe chimwecho kwa maganizo yake mwene, nambho ndande iye wadali mjhukulu wamkulu wachaka chimenecho, wadalosa kuti Yesu siwafe ndande ya jhiko la Ayahudi, 52osati kuti siwamwalile ndande ya Ayahudi okha, nambho ndande ya kwaakusa pamojhi wana Amnungu anyiyao amwazika.
53Ndiipo, kuyambila siku limenelo achogholeli wa Ayahudi adayamba kufunafuna njila ya kumpha Yesu. 54Chimwecho, Yesu siwadaendenjho padanga pakati pa Ayahudi, ndiipo wadachoka pamenepo, ni kupita pafupi ni phululu, mmujhi uwo utanidwa Eflaimu. Wadakhala kumemeneko ni oyaluzidwa wake.
55Pwando la Pasaka la Ayahudi lidawandikila, wandhu ambili adapita ku Yelusalemu kuti akajhieleche likali osajhe pwando limenelo. 56Wandhu amamfunafuna Yesu. Yapo adali pamojhi mu Nyumba ya Amnungu, adafunjhana, “Bwanji mundhu uyu siwafika kupwando?” 57Chimwecho ajhukulu waakulu ni Afalisayo adachocha lamulo kuti mundhu waliyonjhe uyo siwajhiwe uko wali Yesu waakambile dala amgwile.
ទើបបានជ្រើសរើសហើយ៖
Yohana 11: NTNYBL2025
គំនូសចំណាំ
ចែករំលែក
ចម្លង

ចង់ឱ្យគំនូសពណ៌ដែលបានរក្សាទុករបស់អ្នក មាននៅលើគ្រប់ឧបករណ៍ទាំងអស់មែនទេ? ចុះឈ្មោះប្រើ ឬចុះឈ្មោះចូល
The New Testament in Nyanja @The Word for The World International and Nyanja Language translation, 2025. All rights reserved.

: