Vichito 25
25
Poolo wafuna mlandu wake upelekedwe kwa mfumu wamkulu wa ku Loma
1Masiku yatatu pambuyo pa Fesito kulowa mumujhi wa Kaisalia ni kuyamba kulamulila, wadachoka ku Kaisaliya ni kupita ku Yelusalemu. 2Waakulu wa ajhukulu ni achogoleli Achiyahudi adajha kwa Fesito kumpacha mlandu wa Poolo. Adamkambila Fesito, 3kuti wachitile ubwino kwa kumpeleka Poolo ku Yelusalemu, pakuti anyiiwo adafunafuna njila ya kumupha Poolo wakali mnjila. 4Nambho Fesito wadaayangha, “Poolo wachekelezedwa mndende kumeneko ku Kaisaliya, ni ine namwenewake sinipite kumeneko posachedwa. 5Akambileni achogoleli wanu achogozane ni ine kupita ku Kaisaliya, kuti akampache mlandhu kumeneko ngati iye wachita choipa chilichonjhe.”
6Fesito wadakhala nawo masiku ngati nane kapina khumi, ndiipo wadapita ku Kaisaliya ni siku ilo lidachatila wadatanicha bwalo la milandu ni kukhala pampando wake wa lamulo, ni kulamula kuti Poolo wapelekedwe pachogolo pake. 7Poolo yapo wadafika, Ayahudi yawo adachokela ku Yelusalemu adamzungulila, niapeleka milandu yambili ya yaikulu yayo siadakhoze kuyachimikiza kalikonjhe. 8Ndiipo Poolo wadajhiteteza niwakamba, “Ine sinadachite chilichonjhe icho chichuchana ni Thauko la Chiyahudi kapina kuchuchana ni Nyumba ya Mnungu kapina kuchuchana ni lamulo la Mfumu wa ku Loma.”
9Nambho pakuti Fesito wamafuna kwaakondwelecha Ayahudi, wadamfunjha Poolo, “Bwanji, ukhoza kupita ku Yelusalemu kuti nikakulamule kumeneko kuchokana ni milandu iyi?”
10Poolo wadayangha, “Pano naima ni pampando wa lamulo wa Mfumu wa ku Loma, ndeyapo nikhoza kulamulidwa. Mujhiwa kuti sinidachite choipa chilichonjhe kwa Ayahudi. 11Ngati nachita chilichonjhe choipa, icho nifunika kupedwa nalo nivomela kupedwa. Nambho ngati milandu yayo yapelekedwa osati ya uzene, ndekuti palibe uyo wakhoza kunipeleka kwa Ayahudi anyiyawa. Nipembha mnipeleke kwa Mfumu wamkulu wa ku Loma.”
12Basi Fesito yapo wadamaliza kukambichana ni wandhu wake abwalo Wadamkambila Poolo, “Iwe wapembha kumuona Mfumu wa ku Loma, chipano siupite kwa Mfumu wa Kuloma.”
Agilipa wajhichidwa nghani za mlandu wa Poolo
13Pambuyo pakutha masiku yochepa Mfumu Agilipa ni Belinike adapita ku Kaisali kumlandila Fesito kukhala mlamuli wachipano. 14Adakhala kumeneko kwa masiku yambili, Fesito wadakambilana ni mfumu Agilipa nghani za mlandu wa Poolo, niwakamba, “Pali mundhu mmojhi pano uyo wadasiidwa ni Felikisi mundende. 15Yapo nidapita ku Yelusalemu, ajhukulu waakulu ni achogoleli wa Ayahudi adanijhiwicha nghani za Poolo ni kunipembha nimlamule kuti walangidwe. 16Nambho nidaayangha kuti mundhu yapo waphezeka mundhu uyo wali ni mlandu, ife Aloma tilibe mthethe wompeleka kwa wandhu wina kuti wagamulidwe. Poyamba wakomane ni yawo ampacha mlandu maso ni maso ni kupachita ndhawi yojhiteteya pa milandu iyo amushitaki. 17Chimwecho yapo adafika pano pamojhi ni ine sinidachedweche, siku lakawili nidatana bwalo nidalamula mundhu mmeneyo wapelekedwe kuno. 18Anyiwajha adampacha mlandu siadapeleke mau lililonjhe loipa, ngati umo nimaganizila. 19Nambho amatochuchana nghani za kulambila kwao ni nghani za mundhu mmojhi uyo wadamwalila watanidwa Yesu, uyo Poolo wakamba kuti wakali wamoyo. 20Nambho pakuti sinimajhiwe umo ningapachitile, nidamfunjha Poolo ngati wakhoza kupita ku Yelusalemu kuti wakalamulidwe kumeneko. 21Nambho Poolo wadapembha wakhalile mundende pano pa Kaisaliya. Wafuna kuti mlandu wake uvecheledwe ni kulamulidwa ni Mfumu wa ku Loma, ni nidalamula kuti wapenyeleledwe mbaka yapo sinimpeleke kwa Mfumu wamkulu wa Ku Loma.”
22Ndiipo Agilipa wadayangha, “Nidakakonda kumvechela mundhu mmeneyo namwene wake.”
Fesito wadayangha, “Siumvechele mawa.”
23Siku lochatila Agilipa ni Belinike adalandilidwa kwa chimwemwe adalowa mu bwalo la milandu, pamojhi ni waakuluakulu wa asikali ni wandhu ojhiwika bwino amujhi. Ndiipo Fesito wadalamula kuti Poolo wapelekedwe mkati. 24Ndiipo Fesito wadakamba, “Mfumu Agilipa pamojhi ni wonjhe yawo muli pano, mwamuona mundhu uyu! Wandhu wonjhe Achiyahudi anidandaulila nghanimundhu uyu kujha ku Yelusalemu ni pano pa Kaisaliya, niakweza phokoso ni kukamba kuti ifunika waphedwe. 25Ine sinidapheze ni choipa chililichonjhe icho chikhoza kumchita iye kuti waphedwe. Nambho pakuti Poolo mwene wadapembha wajhe kulamulidwa ni Mfumu wa ku Loma, nidalamula kumpeleka ku Loma. 26Nambho ine nilibe uzee uwo nidakakoza kumlembela olemekezedwa amfumu wakulu aku Loma, ndande imeneyo nampeleka pachogolo panu hasa kwaimwe amfumu Agilipa, kuti mkathomaliza kumfujha nane nipate cha kulemba. 27Niganiza siikhala bwino kumpeleka womangidwa kwa Kaisalia popande kumfotokozela bwino ivo walakwa.”
ទើបបានជ្រើសរើសហើយ៖
Vichito 25: NTNYBL2025
គំនូសចំណាំ
ចែករំលែក
ចម្លង
ចង់ឱ្យគំនូសពណ៌ដែលបានរក្សាទុករបស់អ្នក មាននៅលើគ្រប់ឧបករណ៍ទាំងអស់មែនទេ? ចុះឈ្មោះប្រើ ឬចុះឈ្មោះចូល
The New Testament in Nyanja @The Word for The World International and Nyanja Language translation, 2025. All rights reserved.

: