Vichito 2:46-47

Vichito 2:46-47 NTNYBL2025

Masiku yonjhe amakomana mmakhumbi la Nyumba ya Mnungu kwa mtima umojhi. Amadya chakudya pamojhi mmanyumba zao kwa kukondwela ni kwa mtima woyela, niamtamanda Mnungu ni wandhu wonjhe adaakonda atumwi ameneo, siku zonjhe Ambuye amachulucha wandhu yao amaomboledwa.

អាន Vichito 2