Yesu yapo wadaima wadamfunjha wamkaziyo, “Alikuti wajha wandhu akupacha mlandhu? Palibe waliyonjhe uyo wakulamula?”
Wamkazi mmeneyo wadayangha, “Wakulu, palibe waliyonjhe!”
Ndiipo Yesu wadamkambila, “Ata ine sinikulamula. Mapita siudachitanjho machimo.”