Yohana 8:10-11
Yohana 8:10-11 NTNYBL2025
Yesu yapo wadaima wadamfunjha wamkaziyo, “Alikuti wajha wandhu akupacha mlandhu? Palibe waliyonjhe uyo wakulamula?” Wamkazi mmeneyo wadayangha, “Wakulu, palibe waliyonjhe!” Ndiipo Yesu wadamkambila, “Ata ine sinikulamula. Mapita siudachitanjho machimo.”