Mundhu mmeneyo wadamvela Poolo yapo wamalalikila, naye Poolo yapo wadampenyechecha, wadaona kuti mundhu mmeneyo wakhulupilila ni wakhoza kulamichidwa, wadamkambila kokweza mvekelo, “Ima kwa miyendo yako!” Pampajha yujha Mundhu wadalumbha ni kuyamba kuyenda.