Maso yawo yapo yadali yakali kumpenyechecha kumwamba Yesu yapo wamapita, mwachizulumukila wachimuna awili yawo adavala njhalu zoyela adaima pambhepete pawo, adakamba, “Anyiimwe wandhu a ku Galilaya, ndande yanji muima pamenepo uku nimpenya kumwamba? Yesu uyo watengedwa kupita kumwamba, siwajhenjho ngati mujha mwamuwonela niwapita kumwamba.”