1
MACHITIDWE 15:11
Buku Lopatulika
BLP-2018
Koma tikhulupirira tidzapulumuka mwa chisomo cha Ambuye Yesu Khristu, monga iwo omwe.
مقایسه
MACHITIDWE 15:11 را جستجو کنید
2
MACHITIDWE 15:8-9
Ndipo Mulungu, amene adziwa mtima, anawachitira umboni; nawapatsa Mzimu Woyera, monga anatipatsa ife; ndipo sanalekanitse ife ndi iwo, nayeretsa mitima yao m'chikhulupiriro.
MACHITIDWE 15:8-9 را جستجو کنید