MACHITIDWE 15:8-9
MACHITIDWE 15:8-9 BLP-2018
Ndipo Mulungu, amene adziwa mtima, anawachitira umboni; nawapatsa Mzimu Woyera, monga anatipatsa ife; ndipo sanalekanitse ife ndi iwo, nayeretsa mitima yao m'chikhulupiriro.