1
1 AKORINTO 9:25-26
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
BLPB2014
Koma yense wakuyesetsana adzikanizira zonse. Ndipo iwowa atero kuti alandire korona wakuvunda; koma ife wosavunda. Chifukwa chake ine ndithamanga chotero, si monga chosinkhasinkha. Ndilimbana chotero, si monga ngati kupanda mlengalenga
Compare
Explore 1 AKORINTO 9:25-26
2
1 AKORINTO 9:27
koma ndipumpuntha thupi langa, ndipo ndiliyesa kapolo; kuti, kapena ngakhale ndalalikira kwa ena, ndingakhale wotayika ndekha.
Explore 1 AKORINTO 9:27
3
1 AKORINTO 9:24
Kodi simudziwa kuti iwo akuchita makani a liwiro, athamangadi onse, koma mmodzi alandira mfupo? Motero thamangani, kuti mukalandire.
Explore 1 AKORINTO 9:24
4
1 AKORINTO 9:22
Kwa ofooka ndinakhala ngati wofooka, kuti ndipindule ofooka. Ndakhala zonse kwa anthu onse, kuti paliponse ndikapulumutse ena.
Explore 1 AKORINTO 9:22
Home
Bible
Plans
Videos