1
Miyambo 31:30
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
CCL
Nkhope yachikoka ndi yonyenga, ndipo kukongola nʼkosakhalitsa; koma mkazi amene amaopa Yehova ayenera kutamandidwa.
Compare
Explore Miyambo 31:30
2
Miyambo 31:25-26
Mphamvu ndi ulemu zimakhala ngati chovala chake; ndipo amaseka osaopa zamʼtsogolo. Iye amayankhula mwanzeru, amaphunzitsa anthu mwachikondi.
Explore Miyambo 31:25-26
3
Miyambo 31:20
Iye amachitira chifundo anthu osauka ndipo amapereka chithandizo kwa anthu osowa.
Explore Miyambo 31:20
4
Miyambo 31:10
Kodi mkazi wangwiro angathe kumupeza ndani? Ndi wokwera mtengo kuposa miyala yamtengowapatali.
Explore Miyambo 31:10
5
Miyambo 31:31
Mupatseni mphotho chifukwa cha zimene iye wachita ndipo ntchito zake zimutamande ku mabwalo.
Explore Miyambo 31:31
6
Miyambo 31:28
Ana ake amamunyadira ndipo amamutcha kuti wodala; ndipo mwamuna wake, amamuyamikira nʼkumati
Explore Miyambo 31:28