1
Miyambo 30:5
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
CCL
“Mawu ali wonse a Mulungu ndi opanda cholakwika; Iye ndi chishango kwa amene amathawira kwa Iye.
Compare
Explore Miyambo 30:5
2
Miyambo 30:8
Choyamba, mundichotsere kutali nane mabodza ndi chinyengo. Chachiwiri, ndisakhale mʼmphawi kapena munthu wachuma. Koma muzindidyetsa chakudya chondikwanira tsiku ndi tsiku
Explore Miyambo 30:8