Miyambo 31:25-26
Miyambo 31:25-26 CCL
Mphamvu ndi ulemu zimakhala ngati chovala chake; ndipo amaseka osaopa zamʼtsogolo. Iye amayankhula mwanzeru, amaphunzitsa anthu mwachikondi.