1
Miyambo 23:24
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
CCL
Abambo a munthu wolungama ali ndi chimwemwe chachikulu; Wobala mwana wanzeru adzakondwera naye.
Compare
Explore Miyambo 23:24
2
Miyambo 23:4
Usadzitopetse wekha ndi kufuna chuma, ukhale ndi nzeru ya kudziretsa.
Explore Miyambo 23:4
3
Miyambo 23:18
Ndithu za mʼtsogolo zilipo ndipo chiyembekezo chakocho sichidzalephereka.
Explore Miyambo 23:18
4
Miyambo 23:17
Mtima wako usachite nsanje ndi anthu ochimwa, koma uziopa Yehova tsiku ndi tsiku.
Explore Miyambo 23:17
5
Miyambo 23:13
Usaleke kumulangiza mwana; ngati umulanga ndi chikwapu sadzafa.
Explore Miyambo 23:13
6
Miyambo 23:12
Mtima wako uzikhala pa malangizo ndipo makutu ako azimvetsera mawu a chidziwitso.
Explore Miyambo 23:12
7
Miyambo 23:5
Ukangoti wachipeza chumacho uwona posachedwa kuti palibepo. Chumacho chimachita ngati chamera mapiko mwadzidzidzi ndi kuwuluka kunka kumwamba ngati chiwombankhanga.
Explore Miyambo 23:5
8
Miyambo 23:22
Mvera abambo ako amene anakubala, usanyoze amayi ako pamene akalamba.
Explore Miyambo 23:22