1
Miyambo 24:3
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
CCL
Nyumba imamangidwa ndi anthu anzeru, ndipo imakhazikika ndi anthu odziwa zinthu
Compare
Explore Miyambo 24:3
2
Miyambo 24:17
Usamakondwera ndi kugwa kwa mdani wako. Mtima wako usamasangalale iye akapunthwa.
Explore Miyambo 24:17
3
Miyambo 24:33-34
Ukati, “Bwanji ndigone pangʼono,” kapena “Ndiwodzereko pangʼono,” kapenanso “Ndipinde manja pangʼono kuti ndipumule,” umphawi udzafika pa iwe ngati mbala ndipo usiwa udzakupeza ngati munthu wachifwamba.
Explore Miyambo 24:33-34