1
Mlaliki 3:1
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
CCL
Chinthu chilichonse chili ndi nthawi yake, ndi nyengo yake yomwe anayika Mulungu
Compare
Explore Mlaliki 3:1
2
Mlaliki 3:2-3
Nthawi yobadwa ndi nthawi yomwalira, nthawi yodzala ndi nthawi yokolola. Nthawi yakupha ndi nthawi yochiritsa, nthawi yogwetsa ndi nthawi yomanga.
Explore Mlaliki 3:2-3
3
Mlaliki 3:4-5
Nthawi yomva chisoni ndi nthawi yosangalala, nthawi yolira maliro ndi nthawi yovina. Nthawi yotaya miyala ndi nthawi yokundika miyala, nthawi yokumbatirana ndi nthawi yoleka kukumbatirana.
Explore Mlaliki 3:4-5
4
Mlaliki 3:7-8
Nthawi yongʼamba ndi nthawi yosoka, nthawi yokhala chete ndi nthawi yoyankhula. Nthawi yokondana ndi nthawi yodana, nthawi ya nkhondo ndi nthawi ya mtendere.
Explore Mlaliki 3:7-8
5
Mlaliki 3:6
Nthawi yofunafuna ndi nthawi yoleka kufunafuna, nthawi yosunga ndi nthawi yotaya.
Explore Mlaliki 3:6
6
Mlaliki 3:14
Ndikudziwa kuti chilichonse chimene Mulungu amachita chidzakhala mpaka muyaya; palibe zimene zingawonjezedwe kapena kuchotsedwa. Mulungu amazichita kuti anthu azimuopa.
Explore Mlaliki 3:14
7
Mlaliki 3:17
Ndinalingalira mu mtima mwanga kuti; “Mulungu adzaweruza olungama pamodzi ndi oyipa omwe, pakuti anayika nthawi yochitikira chinthu chilichonse, nthawi ya ntchito iliyonse.”
Explore Mlaliki 3:17