Alom 4
4
Chifani cha Ibulahimu
1Tikambe chiyani chipano, nghani za Ibulahimu tate wathu iye ngati mundhu, wadajhiwa bwanji chindhu ichi cha kuvomelezeka pachogolo pa Mnungu? 2Ngati Ibulahimu wadali wovomelezeka kwa Mnungu ndande ya mbhavu zake, basi wali ni chindhu chojhidamila pachogolo pa Mnungu. 3Pakuti malembo yoyela yakamba, “Iblahimu wadaakhulupilila Amnungu, nawo Amnungu adamvomela kukhala ovomwelezeka.” 4Uyo wachita njhito walipidwa mkokolo wake, osati mbhaso nambho ni kuvomelezeka kwake. 5Nambho mundhu uyo siwakhulupilila vichito vake mwene, nambho wakhulupila Mnungu uyo walekeleledwa voipa, chimwecho Mnungu wasamala chikhulupi cha mundhu mmeneyo, ni kumvomela kukhala woyela. 6Naye Daudi wakambanjho chimwecho ndande ya kukondwa uko walinako mundhu uyo wavomelezedwa ni Mnungu kuti ni woyela, popande kukhulupilila vichito vake,
7“Sakondwele wandhu yawo alekeleledwa machimo yao,
yawo machimo yao vafutidwa.
8Siwakondwele kupunda mundhu yujha, Ambuye sayakumbukila machimo yake!”
9Bwanji kukondwela kumeneko kukambidwa ni Daudi ni kwaanyiwajha achitidwa mdulidwepe mate yake Ayahudi, kapina ni kwaanyiwajha siadachitidwe mdulidwe mate yake wandhu yawo osati Ayahudi? Ni kwaanyiwajha sadachitidwe mdulidwe. Pakuti tathokamba, “Ibulahimu wadaakhulupilila Amnungu, niiwo Amnungu adamvomele kukhala woyela wakali siwadachitidwe mtulidwe.” 10Bwanji Ibulahimu wadavomelezeka ni Mnungu wakali siwadachitidwe mdulidwe Kapina yapo wadachitidwa mdulidwe? Yapo wadali wakali siwadachitidwe mdulidwe niosati yapo wadachitidwa mdulidwe. 11Iblahimu wadachitidwa mdulidwe pambuyo, ni chikuchitidwa mdulidwe kumeneko kudali chizindikilo icho chidalangiza kuti Mnungu wadamvomela kukhala wa bwino, ndande ya chikhulupi chake icho wadali nacho yapo wadali wakali siwadachitidwe mdulidwe. Mchimwecho, Ibulahimu wakhala tate wa wajha wonjhe amkhulupilila Mnungu ingakale siadachitidwe mdulidwe, kuti ata anyiiwo avomelezeke pachogolo pa Mnungu. 12Chimchijha Ibulahimu ni tate wa anyiwajha achitidwa mdulidwe, nambho osati ndande achitidwa mdulidwe, nambho ndande adakhulupilila ngati umo wadakhulupilila tate wathu Ibulahimu yapo adali akali sadachitidwe mdulidwe.
Yajha wakamba Mnungu kuti siwatipache yapezeka kwa kukhulupilila
13Mnungu wadamkambila Ibulahimu ni mbadwa wake kuti jhiko lidakakhala lao. Ahadi imeneyo sidachitike ndande Ibulahimu wadachata Thauko, nambho ndande wadakhulupilila Mnungu ndiipo Mnungu wadamchita kukhala wa bwino. 14Pakuti ngati yawo sapachidwe yayo ayakamba Amnungu niwajape avela thauko, chimwecho chikhulupi chilibe mate yaliyonjhe, ni icho achikamba Amnungu osati chindhu cha mate. 15Thauko lipeleka mbhwayi ya Mnungu, nambho ngati kulibe thauko siikhozekena kuliwananga thauko.
16Ndande imeneyo, chindhu ichi wakamba Mnungu kuti siwachite likhulupilila kumkhulupilila iye, mawu yameneyo yakambidwa ni Mnungu yachokana ni ubwino wake, ni zene kuti yajha wayakamaba kuti siwatipache, siwatipache wonjhe, niosati kwaanyiwajhape avela thauko, nambho ni anyiwajha akhala kwa kumkhulupilila Mnungu ngati Ibulahimu. Iye ni tate waife taonjhe. 17Ngati umo yalembedwela mmalembo ya Mnungu, “Nakuika ukhale tate wa wandhu a maiko yambili.” Mawu yameneyo ni ya uzene pachogolo pa Mnungu uyo wadamkhulupilila Ibulahimu, Mnungu uyo waapacha wandhu akufa umoyo, ni kwa lamulo lake vindhu ivo sividakhalepo vikhalapo. 18Ibulahimu pajha wadakambidwa mawu yajha yadali yolimba kuyakhulupila, nambho Ibulahimu wadaendekela kukhulupilila kuti Mnugnu siwamchite kukhala tate wa wandhu a maiko yambili, ngati umo yalembedwa mmalembo, “Mibadwa yako siikhale yambili ngati ndhondwa!” 19Wadali mzee, ni vyaka vake vidawandikila miya mojha nambho pamojhi ni chimenecho chikhulupililo chake sichidachepekele ata ngati wadajhiwa kuti siwakhozanjho kupata mwana thupi lake lidali ngati lafa ni mkazake sala wadali wambende. 20Ibulahimu siwadakhaikile lijha lidakambidwa ni Mnungu, wadapata mbhavu kuchokana ni chikhulupililo, wadayendekela kumkhulupilila ni kumpacha ulemelelo. 21Ibulahimu wadajhiwa zenedi kuti Mnungu wakhoza kuyakwanilicha yajha wadakamba kuti siwatipache. 22Iyi ndendande iyo Mnungu wadamvomelela Ibulahimu kukhala wabwino. 23Chimwecho mawu yaya yalembedwa kuti, “Mnungu wadamvomela Ibulahimu kukhala wabwino” Siyadalembedwe ndande yaiyepe. 24Nambho chindhu chimecho ni cha ife timkhulupilila Mnungu uyo wadamuhyukicha Yesu, Ambuye wathu. 25Iye wadachochedwa wapedwe ndande ya machimo yathu, wadahyuka ndande ife tivomelezeke.
ទើបបានជ្រើសរើសហើយ៖
Alom 4: NTNYBL2025
គំនូសចំណាំ
ចែករំលែក
ចម្លង
ចង់ឱ្យគំនូសពណ៌ដែលបានរក្សាទុករបស់អ្នក មាននៅលើគ្រប់ឧបករណ៍ទាំងអស់មែនទេ? ចុះឈ្មោះប្រើ ឬចុះឈ្មោះចូល
The New Testament in Nyanja @The Word for The World International and Nyanja Language translation, 2025. All rights reserved.

: