Alom 4:18

Alom 4:18 NTNYBL2025

Ibulahimu pajha wadakambidwa mawu yajha yadali yolimba kuyakhulupila, nambho Ibulahimu wadaendekela kukhulupilila kuti Mnugnu siwamchite kukhala tate wa wandhu a maiko yambili, ngati umo yalembedwa mmalembo, “Mibadwa yako siikhale yambili ngati ndhondwa!”

អាន Alom 4