Alom 2:3-4

Alom 2:3-4 NTNYBL2025

Nambho iwe ulamula wandhu yawo achita vindhu voipa ngati umo uchitila umwene, uganiza kuti ukhoza kulithawa lamulo la Mnungu? Kapina upepula kuchuluka kwa ubwino wake waukulu, kulimba kwake mtima ni kulindilila kwake, siujhiwa kuti ubwino wake umenewo uli ni ndande ya kukuchogoza iwe kuti ulape?

អាន Alom 2