Yohana 8
8
Wamkazi uyo wadagwilidwa niwachita chigololo
1Chimwecho Yesu wadapita mbaka ku Phili la Mizeituni. 2Mawa lake umawa wadapita kunyumba ya Amnungu. Wandhu ambili adamzungulila, chimwecho wadakhala ni kuyamba kwayaluza. 3Ndiipo, oyaluza Thauko ni Afalisayo adajhanayo wamkazi mmojhi uyo wadagwilidwa uku ni wachita chigololo. Adamuimika pachogolo pao. 4Ndiipo adamfunjha Yesu, “Oyaluza, wamkazi uyu wagwilidwa ni wachita chigololo. 5Muthauko, Musa wadatilamula wamkazi ngati uyu wabulidwe miyala mpaka kumwalila. Imwe mkamba bwanji?” 6Adamuyesa kokamba chimwecho, kuti ampache mlandu. Nambho Yesu wadakwatama panjhi ni kulemba pa ndhaka kwa chala chake.
7Yapo adapunda kumfunjha, wadaima nikwakambila, “Mundhu waliyonjhe uyo walibe machimo pakati panu wakhale oyamba kumbula mwala.” 8Wadakwatamanjho ni kulemba pandhaka kwa chala chake. 9Yapo adavela chimwecho adayamba kuchoka mmojhimmojhi, adachogola azee. Wadakhalila Yesu yokha ni wamkazi waima pachogolo pake. 10Yesu yapo wadaima wadamfunjha wamkaziyo, “Alikuti wajha wandhu akupacha mlandhu? Palibe waliyonjhe uyo wakulamula?”
11Wamkazi mmeneyo wadayangha, “Wakulu, palibe waliyonjhe!”
Ndiipo Yesu wadamkambila, “Ata ine sinikulamula. Mapita siudachitanjho machimo.”
Yesu ni dangalila la wandhu ajhiko
12Ndiipo Yesu wadaakambilanjho, “Ine nde dangalila la jhiko la panjhi. Uyo wanichata siwaenda mu mdima, nambho siwakhale ni dangalila la umoyo.”
13Chimwecho Afalisayo adamkambila, “Umboni wako osati wazene, ndande ujhichochela umboni umwene.”
14Yesu wadayangha, “Atangati nikajhichochela umboni namwene, umboni wanga wazene ndande nijhiwa uko nichoka ni uko nipita. Nambho anyiimwe simujhiwa uko nichoka ni uko nipita. 15Anyiimwe mulamula ngati umo wandhu alamulila, nambho ine sinimlamula mundhu waliyonjhe. 16Ata ngati nikalamula, lamulo langa ni lazene ndande ine sinilinekha, nambho nilamula pamojhi ni Atate yao anituma. 17Yalembedwa mu Thauko lanu umboni wa wandhu awili uvomelezeka. 18Ine nijhichochela umboni namwene wake, ni Atate yao anituma, anichochela umboni.”
19Ndiipo adamfunjha, “Atate wako alikuti?”
Yesu wadaayangha, “Anyiimwe simunijhiwa ine nambho Atate wanga ndeyawo anijhiwa. Ngati mdakanijhiwa ine, mudakaajhiwa Atate.”
20Yesu wadakamba mawu yameneyo yapo wamayaluza Mnyumba ya Amnungu wali pafupi ni bokosi lo sungila njhembe. Palibe uyo wadamgwila, ndande ndhawi yake idali ikali.
Uko nipita anyiimwe simukhoza kufika
21Yesu wadaakambilanjho, “Ine nipita, namwe simunifunefune, nambho simufe mumachimo yanu. Uko nipita ine, anyiimwe simukhoza kufika.”
22Ndiipo achogholeli wa Ayahudi adakamba, “Bwanji siujhiphe? Mbona ukamba, ‘Uko nipita anyiimwe simukhoza kufika?’”
23Yesu wadaakambila anyiwajha ochogoleli Ayahudi, “Anyimwe mchokela pano pajhiko la panjhi, nambho ine nachoka kumwamba kwa Amnungu. Anyiimwe ajhiko lino la panjhi, nambho ine osati wajhiko lino. 24Ndendande nidakukambilani kuti simufe mumachimo yanu. Ngati mkasiya ku khulupilila kuti ‘Ine nde mwene,’ simufe mu machimo yanu.”
25Nawo adamfunjha, “Iwe ni yani?”
Yesu wadaayangha, “Ine ni yujha nidakukambilani kuyambila mmayambo! 26Nili nimawu yambili ya kukukambilani ni ya kukulamulani. Nambho uyo wanituma wazene, nane nilikambila jhiko mawu yayo nayavela kuchokela kwaiye.”
27Siamajhiwe kuti, Yesu wamakamba nawo nghani za Atate. 28Ndiipo, Yesu wadakambila, “Yapo simumpachike mumtengo Mwana wa Mundhu, nde yapo simujhiwe kuti, ‘Ine nde Mwene,’ ni sinichita chilichonjhe nekha, nambho niyakambape yajha Atate aniyaluza. 29Uyo wanituma walipamojhi nane, iye siwadanisiye nekha pakuti sikuzonjhe nichita yajha yamkwadilicha.”
30Yapo wadakamba yameneyo wandhu ambili adamkhulupilila.
Uzene siukulekeleleni
31Ndiipo, Yesu wadaakambila Ayahudi yawo adamkhulupilila, “Mkayagwila mayaluzo yanga simukhale oyaluzidwa wanga azene. 32Simuujhiwe uzene, ni uzene siukulekeleleni.”
33Nawo adayangha, “Ife mibadwa ya Ibulahimu, sitidakhalepo akapolo amundhu waliyonjhe. Ukamba bwanji kuti, ‘Sitilekeledwe?’”
34Yesu wadayangha, “Uzene nikukambilani, uyo wachita machimo ni kapolo wa machimo. 35Kapolo walibe pokhala polimba pakhomo, nambho mwana wali ni pokhala. 36Mwana wakakuchitani mlekeleledwe simulekeleledwe zenezene. 37Nijhiwa kuti anyiimwe mibadwa ya Ibulahimu. Ata chimwecho, mufuna kuniipha ndande mawu yanga siyapata malo mmitima mwanu. 38Ine nikukambilani yayo nayaona kuchoka kwa Atate wanga, anyiimwe chinchijha muchita yayo mwayavela kuchoka kwa atate wanu.”
39Ndiipo adamuyangha, “Ife atate wathu Ibulahimu!”
Yesu wadakambila, “Ngati mudakali wana a Ibulahimu, mdakachita yajha wadachita Ibulahimu. 40Nambho anyiimwe mfuna kuniipha, mundhu uyo nakukambilani uzene kuchoka kwa Amnungu, Ibulahimu siwadachite chimwecho! 41Anyiimwe muchita vindhu ivo achita Atate wanu.” Ndiipo adakambila, “Ife sitidabadwe muchigololo! Tilinawo Atate amojhipe, nde Amnungu.”
Ndiipo adamkambila, “Ife sitidabadwe muchigololo! Tilinawo Atate amojhipe, nde Amnungu.”
42Yesu wadakambila, “Ngati Amnungu adakali Atate wanu, mdakanikonda ine, ndande ine nachoka kwa Amnungu ni chipano nilipano. Sinidajhe kwa lamulo langa namwene, nambho najha kwa lamulo la uyo wanituma. 43Ndande yanji simuvana navo ivo nikukambilani? Ndande simukhoza sikuyasikiliza mayaluzo yanga. 44Anyiimwe ni wana a tate wanu Satana, ni mufunape kuchita makhumbilo ya Atate wanu. Iye wakupha kuyambila mmayambo, siwaima pa uzene, ndande walibe uzene mkati mwake. Yapo wakamba unami wakamba kuchokana ni umowali mwene, pakuti iye waunami ni tate wa unami umeneo. 45Ine yapo nikamba uzene anyiimwe simunikhulupilila. 46Yani pakati panu wakhoza kuchimikiza kuti ine nili ni machimo? Ngati nikukambilani uzene ndande yanji simunikhulupilila? 47Waliyonjhe uyo wachoka kwa Amnungu wayavechela mawu ya Amnungu. Nambho anyiimwe simukhulupilila ndande simchoka kwa Amnungu.”
Yesu wadalipo Ibulahimu wakali osakhalepo
48Ayahudi adamfunjha Yesu, “Bwanji, osati zene yapo tikamba iwe Msamalia, ni kuti uli ni viwanda?”
49Yesu wadayangha, “Ine nilibe viwanda, nambho nalemekeza Atate wanga, anyiimwe simunilemekeza. 50Sinijhifunila ulemelelo wanga namwene, walipo mundhu wanifunila funila iye nde mlamuli. 51Nikukambilani uzene, uyo wavela mawu yanga siwamwalila muyaya.”
52Ndiipo, Ayahudi adakamba, “Sazino tajhiwa zenedi uli ni viwanda! Ibulahimu wadamwalila, ni alosi nawo adamwalila, ni iwe ukamba kuti waliyonjhe uyo wavela mawu yanga simmwalila muyaya! 53Bwanji iwe ni wamkulu kulekana ni atate wathu Aibulahimu yawo adamwalila? Alosi adamwalila. Iwe uganiza kuti ni yani?”
54Yesu wadayangha, “Nikajhipacha namwene ulemelelo, ulemelelo wanga ulibe mate. Yao anipacha ulemelelo, nde Amnungu yawo mwaakamba anyiimwe kuti Atate wanu. 55Anyiimwe simwajhiwa, nambho ine najhiwa. Sinikhale waunami ngati anyiimwe ni kakamba kuti sinajhiwa. Nambho ine najhiwa ni nichita icho achikamba. 56Ibulahimu, tate wanu, wadakondwela walione siku langa, ni wadaiona, nayo wadakondwela.”
57Ndiipo, Ayahudi adaamkambila, “Iwe ukali siuda kwanile vyaka hamsini, wamuona kuti Ibulahimu?”
58Yesu wadaakambila, “Zene nikukambilani, Ibulahimu wakali osakhalepo, ine nidalipo.”
59Chimwecho adatondola miyala kuti amponyele, nambho Yesu wadatuluka Mnyumba ya Amnungu ni kujhibisa.
ទើបបានជ្រើសរើសហើយ៖
Yohana 8: NTNYBL2025
គំនូសចំណាំ
ចែករំលែក
ចម្លង

ចង់ឱ្យគំនូសពណ៌ដែលបានរក្សាទុករបស់អ្នក មាននៅលើគ្រប់ឧបករណ៍ទាំងអស់មែនទេ? ចុះឈ្មោះប្រើ ឬចុះឈ្មោះចូល
The New Testament in Nyanja @The Word for The World International and Nyanja Language translation, 2025. All rights reserved.

: