Yohana 21
21
Yesu waachokela oyaluzidwa saba
  1Pambuyo pa yameneyo, Yesu wadaachokela oyaluzidwa wake muchijha la nyanja Tibelia. Wadaachokela chimwechi. 2Simoni Petulo, Tomaso uyo wamatanidwa Mawila, Nasanaeli mundhu wa ku Kana ya Galilaya, wana awili a Zebedayo ni oyaluzidwa wake wina awili, adali onjhe pamojhi.
  3Simoni Petulo wadaakambila achaanjake, “Nipita kuvuwa njhomba.”
Nao adaamkambila, “Tipita taonjhe kuvuwa.” Ndiipo adapita, adakwela mbwato, nambho usiku umeneo sadapate kandhu. 4Malenga kucha, Yesu wadaima mbhepete mwa nyanja, nambho oyaluzidwa sadajhiwe kuti nde Yesu. 5Ndiipo, Yesu wadaafunjha, “Anyamata wanga, simudapate njhomba yaliyonjhe?”
Adayangha, “Sitidapate kandhu.”
  6Yesu wadaakambila, “Chichani khokha bendeka lakwene la bwato simupate njhomba.” Ndiipo adaponya khokha bendeka limwelo nambho adalepela kuguza ndande ya kuchuluka kwa njhomba.
  7Chimwecho yujha oyaluzidwa wamakondedwa kupunda ni Yesu, wadamkambila Petulo, “Ekee Ambuye!” Simoni Petulo yapo wadavela kuti Ambuye, wadavala njhalu yake, ndande siwadavale njhalu, ni kujhitaya mmajhi. 8Nambho anyiwajha oyaluzidwa wina yawo adali pamtunda, adajha pa bwato uku niaguza khokha lojhala njhomba, adali ngati utali mita mia kuchoka pamtunda. 9Yapo adafika pamtunda adapheza moto wa makala wasonghedwa, njhomba niziochedwa ni bumunda. 10Yesu wadaakambila, “Majhanazoni njhomba zakumojhi izo mwavuwa.”
  11Chimwecho, Simoni Petulo wadakwela mubwato, wadaguza khokha limenelo mbaka kumtunda lidajhala njhomba zazikulu mia imojhi ni hamsi ni zitatu. Atangati njhomba zidachuluka, sizidang'ambe khokha. 12Yesu wadaakambila, “Majhani mudye chakudya cha umawa.” Palibe waliyonjhe uyo wadayesa kumfunjha kuti, “Iwe yani?” Ndande adajhiwa adali Ambuye. 13Yesu wadajha, wadatenga bumunda, wadapacha, ni zijha njhomba wadachita chimwecho.
  14Imene idali mala ya katatu Yesu kwachokela oyaluzidwa wake pambuyo po hyuka.
Yesu wampacha maagizo Petulo
  15Yapo adadya, Yesu wadamfunjha Simoni Petulo, “Simoni Petulo mwana wa Yohana! Bwanji, unikonda ine kupitilila anyiyawa?”
Nayo wadayangha, “Etu, Ambuye, mujhiwa nikukondani.”
Yesu wadamkambila, “Dyecha gulu la mbelele zanga.” 16Ndiipo Yesu wadamfujhanjho kakawili, “Simoni mwana wa Yohana! Bwanji, unikonda?”
Petulo wadayangha, “Etu, Ambuye, mujhiwa nikukondani.”
Yesu wadamkambila, “Sunga mbelele zanga.” 17Wadamfunjha kakatatu, “Simoni mwana wa Yohana! Bwanji, unikonda?”
Petulo wadadandaula kupunda ndande wadamfunjha katatu, “Unikonda?” Wadamkambila, “Ambuye, imwe mujhiwa yonjhe, mujhiwa kuti nikukondani.”
Yesu wadamkambila, “Dyecha gulu la mbelele zanga. 18Zene nikukambila, yapo udali mnyamata udavala wamwene lamba lako mchiuno ni kupita uko ufuna. Nambho yapo siukhale mdala siutambasule manja yako ni mundhu mwina siwakuveke lamba ni kukupeleka uko siufuna kupita.” 19Yapo wadakamba chimwecho, wamalangiza umo siwafele Petulo ni kumpacha ulemelelo Mnungu. Ndipo wadamkambila, “Nichate.”
Yesu ni yujha Oyaluzidwa mwina
  20Petulo yapo wadang'anamuka, wadamuona yujha wakondedwa ni Yesu wachata, mmeyo nde yujha oyaluzidwa uyo wadagona pamtima pa yesu yapo amadya chakudya ndhawi ya usiku, wadamfunjha Yesu, “Ambuye, yani uyo siwakung'anamukeni?” 21Petulo yapo wadamuona oyaluzidwa mwinayo, wadamfunjha Yesu, “Ambuye chindhu chanji sichimchokele uyu?”
  22Yesu wadamuyangha, “Ngati nifuna wakhale moyo mbaka yapo sinijhe, iwe ikuusu chiyani? Iwe nichate ine”
  23Chimwecho, nghani idaenela pakati oyaluzidwa wina kuti oyaluzidwa mmeneyo siwamwalila. Nambho Yesu siwadaakambile kuti oyaluzidwa mmeneyo siwafa, nambho, “Ngati nifuna wakhale moyo mbaka yapo sinijhe, iwe ikuusu chiyani? Iwe nichate ine”
  24Mmeneyo nde yujha oyaluzidwa wadayaona yaya ni kuyalemba. Nafe tijhiwa kuti yayo wayakamba ya zene.
Kuthela
  25Kuli ni vindhu vambili ivo wadachita Yesu, ngati yadakalembedwa yonjhe, lina palina, niganiza jhiko silidakakwana kuvisunga vikalakala ivo vidakalembedwa.
      ទើបបានជ្រើសរើសហើយ៖
Yohana 21: NTNYBL2025
គំនូសចំណាំ
ចែករំលែក
ចម្លង

ចង់ឱ្យគំនូសពណ៌ដែលបានរក្សាទុករបស់អ្នក មាននៅលើគ្រប់ឧបករណ៍ទាំងអស់មែនទេ? ចុះឈ្មោះប្រើ ឬចុះឈ្មោះចូល
The New Testament in Nyanja @The Word for The World International and Nyanja Language translation, 2025. All rights reserved.

: