Yohana 19:36-37
Yohana 19:36-37 NTNYBL2025
Yameneyo yadachokela dala yakwanile Malembo Yoyela, yayo yadakamba, “Palibe chifupa chake ata chimojhi icho sichithyoledwe.” Ndiipo maleombo ina yakambanjho, “Sampenye uyo adamlasa ni msongha.”