Yohana 19:26-27
Yohana 19:26-27 NTNYBL2025
Yesu yapo wadaona amake aima pafupi ni oyaluzidwa uyo wamamkonda, wadaakambila amaye wake, “Maye! Mwana wanu uyo yapo.” Ndiipo wadamkambila yujha oyaluzidwa wake Yohana, “Amaye wako yawo yapo.” Kuyambila ndhawi imeneyo oyaluzidwayo wadatengedwa ni amaye wake Ayesu kukhala kukhomo kwao.