Vichito 25:6-7

Vichito 25:6-7 NTNYBL2025

Fesito wadakhala nawo masiku ngati nane kapina khumi, ndiipo wadapita ku Kaisaliya ni siku ilo lidachatila wadatanicha bwalo la milandu ni kukhala pampando wake wa lamulo, ni kulamula kuti Poolo wapelekedwe pachogolo pake. Poolo yapo wadafika, Ayahudi yawo adachokela ku Yelusalemu adamzungulila, niapeleka milandu yambili ya yaikulu yayo siadakhoze kuyachimikiza kalikonjhe.

អាន Vichito 25