Mt. 24:9-11

Mt. 24:9-11 BLY-DC

“Pambuyo pake anthu adzakuperekani kuti mukazunzidwe, kenaka adzakuphani. Anthu a mitundu yonse ya anthu adzadana nanu chifukwa cha Ine. Pa nthaŵi imeneyo ambiri adzataya chikhulupiriro chao, azidzaperekana nkumadana. Kudzaoneka aneneri onama ambiri, amene azidzasokeza anthu ambiri.

مطالعه Mt. 24