YouVersion Logo
Search Icon

Alom 10

10
1Achabale wanga, nifuna ni kulindilila kwa mtima wanga wonjhe achameneo a Izilaeli anjanga aomboledwe. Naapembela kwa Mnungu siku zonjhe. 2Pakuti nikhoza kukamba padanga kuti anyiiwo achita njhito yaikulu ya kumfunafuna Mnungu, nambho njhito imeneyo siidamangidwe pamwamba pa kujhiwa kwa zene. 3Saadajhiwe umo Mnungu waachitila wandhu avomelezeke kwa iye. Chimwecho wandhu ayesa kuyambicha mitundu yawo achinawene, ni chimwecho aikana njila ya Mnungu ya kwachita kukhala ovomelezeka. 4Chimwecho kwakujha kwake kilisito, walichita thauko silidakhala chindhu cho khulupilika pakwachita wandhu kukhala ovomelezeka, nambho wandhu avomelezeka ni Mnungu kwa njila ya kumkhulupilila Kilisito.
Uwomboli uli ndande ya wandhu wonjhe
5Kwa nghani yakuvomelezeka pachogolo pa Amnungu kwa kuchata thauko, Musa wadalemba chimwechi, “Mundhu waliyonjhe uyo wachita ngati umo lifunila thauko siwakhale kwa kuchata thauko limenelo.” 6Nambho kwa nghani zovomelezeka ni Mnungu kwa njila ya chikhulupi, ikambidwa chimwechi, “Siudakamba mumtima mwako, yani siwakwele mbaka kumwamba?” Kukamba chimwecho nde ngati kujhanayo Kilisito panjhi. 7Ndipo mukamba, “Yani siwachike mbaka kumalo ya wandhu akufa? Kumeneko nde ngati kukamba kujhanayo kilisito kuchoka kwa kujhiko la wandhu akufa.” 8Malembo ya Mnungu yakamba chimwechi, “Uthenga umeneo wa Mnungu uli pafupi ni iwe, uli mkamwa mwako ni mumtima mwako” Nayo nde chijha chikhulupi tilalikila. 9Ngati ukakamba kwa pakamwa pako kuti Yesu ni Mbuye, ni kukhulupilila mumtima mwako kuti Mnungu wadamuhyukicha, siuomboke. 10Pakuti mundhu wakhulupilila kwa mtima ni kuvomelezeka pachogolo pa Mnungu, ni kukamba mwene kwa pakamwa pake wakhoza kuomboledwa. 11Yalembedwa mmalembo ya Mnungu, “Waliyonjhe uyo wakhulupilila Kilisito siwalenga njhoni.” 12Chindhu ichi ni kwa wonjhe, pakuti balibe kusiyana kwa Ayahudi ni anyiawo osati ayahudi, Mbuye wa wonjhe ni mmojhi, naye wali ni ubwino kupunda kwa wandhu ampembha. 13Yalembedwa chimwechi mmalembo ya Mnungu, “Mundhu waliyonjhe uyo siwapembhe kwa ulamuli wa jhina la Ambuye siwaomboledwe.”
14Chipano sampembhe bwanji iye samkhulupilila? Nianyiiwo, samkhulupilile bwanji ngati sadavela nghani zake? Nisavele bwanji ngati palibe mundhu olalikila? 15Ni wandhu salalikile bwanji ngati sadapelekedwe? Ngati umo yalembedwa mmalembo ya Mnungu, “Chindhu chokwada kupunda kujha kwa wajha alalikila Uthenga Wabwino!” 16Nambho asati wonjhe adaulandila Uthenga Wabwino. Nde ndande Isaya wadakamba, “Mbuye ni yani uyo wadakhulupilila uthenga wathu?” 17Chimwecho, chikhulupi chichokana ni kuvela Uthenga Wabwino, ni uthenga umeneo uchokana ni mawu la Kilisito.
18Nambho nifunjha, bwanji sadauvele uthenga umenewo? Zenedi adauvela, ngati umo malembo ya Mnungu yakambila,
“Wandhu alalikila Uthenga Wabwino mjhiko lonjhe,
ni uthenga wao wafika mbaka mmathelo mwa jhiko.”
19Nane nifunjhanjho, bwanji a Izilaeli sadajhiwe? Musa mwene wadali woyamba kuyangha,
“Sinikuchiteni mwaonele njhanjhe,
wandhu anyiawo osati jhiko langa,
sinikuchiteni mkhale ni mbhwayi,
kwa jhiko la wandhu asabobwa.”
20Isaya wakamba,
“Nidaphezekana kwa anyiawo sadanifunefune,
najhilangiza kwa wandhu yao sadanifunefune.”
21Nambho kwa nghani za Izilaeli Mnungu wadakamba, “Usana wonjhe nidaima kuti naalandile wandhu opanduka ni osavela.”

Currently Selected:

Alom 10: NTNYBL2025

Highlight

Share

Copy

None

Want to have your highlights saved across all your devices? Sign up or sign in