YouVersion Logo
Search Icon

Matayo 26

26
Upandu wa kumpha Yesu
Maluko 14:1,2; Luka 22:1,2; Yohana 11:45-53
1Yesu yapo wadamaliza kuyaluza yonjhe, wadaakambila oyaluzidwa wake, 2“Ngati umo mjhiwila kuti pambuyo pa masiku yawili sikukhale pwando la Pasaka, ni Mwana wa Mundhu siwapelekedwe kwa adani wake kuti wapachikidwe pamtanda.”
3Ndiipo ajhukulu wakulu ni wakulu a wandhu adakomana pamojhi mnyumba ya milandhu wa Mjhukulu Wamkulu uyo watanidwa Kayafa, 4adakambilana upandu wa kumgwilila Yesu kwa chisisi kuti amphe. 5Anyiiwo adakambilana, “Siifunika tichite chimwechi ndhawi ya phwando la Pasaka, wamdhu siadachita mkanganjili pakati pa wandhu.”
Yesu wapungulilidwa mafuta ku mujhi wa Besania
Maluko 14:3-9; Yohana 12:1-8
6Yesu wadali ku Besania mnyumba mwa Simoni uyo wadali ni makate. 7Yesu yapo wamadya, wadajha wamkazi mmojhi uyo wadasenjhela njhupa ya mafuta yonunghila ya mtengo waukulu, wadayapungulila pamutu pa Yesu. 8Oyaluzidwa wake yapo adaona chimwecho adakwiya, adafunjhana, “Ndande chiani wayawananga chimwechi mafuta yaya? 9Mafuta yonunghila yaya yadakakhoza kugulichidwa kwa mtengo waukulu ni ndalama kwaapacha osauka!”
10Yesu wadajhiwa icho amakamba, wadaakambila, “Ndande yanji mumchaucha wamkaziyu? Uyu wamkazi wanichitila chindhu chabwino kupunda. 11Osauka simukhale nawo masiku yonjhe, nambho ine simukhala nane masiku yonjhe. 12Yapo wanipungulila mafuta yaya pathupi, wachita chimwecho dala kukonjekela kuzikidwa kwanga. 13Zenedi nikukambilani, kulikonjhe uko kulalikidwa uthenga wabwino, chindhu ichi wachichita wamkazi huyu sichilalikilidwe kwa kumkumbukila iye.”
Yuda wavomela kumng'anamuka Yesu
Maluko 14:10-11; Luka 22:3-6
14Ndiipo mmojhi wa anyiwajha oyaluzidwa khumi ni awili, uyo wamatanidwa Yuda isikaliote wadapita kwa wakulu a jhukulu, 15wadaafunjha, “Simunipache ndalama zingati nikamng'anamuka Yesu kwanu?” Chimwecho adamuwelengela magelenjha selasini ni kumpacha. 16Kuyambila pamenepo Yuda wamafunafuna mtundu wabwino wa kumng'anamuka Yesu.
Yesu wakudya chakudya cha Pasaka pamojhi ni oyaluzidwa wake
Maluko 14:12-21; Luka 22:7-13,21-23; Yohana 13:21-30
17Msiku loyamba la pwando la mabumunda yayo yalibe amila, oyaluzidwa adajha kwa Yesu ni kumfunjha, “Ufuna tikakukonjekele kuti chakudya cha pwando la Pasaka?”
18Yesu wadaayangha, “Pitani mmujhi kwa wammuna mmojhi, mukamkambile, ‘Oyaluza akamba, saa yanga yafika, ine ni oyaluzidwa wanga sitidye chakudya cha Pasaka mnyumba yako.’ ”
19Oyaluzidwa adachita ngati umo Yesu wadaakambila, adakonja chakudya cha pwando la Pasaka.
20Yapo udafika ujhulo, Yesu ni oyaluzidwa wake khumi ni awili adakhala kudya chakudya. 21Yapo amadya, Yesu wadaakambila, “Zenedi nikukambilani, mmojhi wanu siwaning'anamuke.”
22Oyaluzidwa wake adavachisoni kupunda, adayamba kumfunjha mmojhimmojhi, “Ambuye, bwanji, ni ine?”
23Yesu wadayangha, “Mundhu mmojhi uyo wasunjha bumunda lake mmbale pamojhi ni ine, nde uyo siwaning'anamuke. 24Mwana wa Mundhu siwamwalile ngati mujha idalembeledwela mu malembo. Nambho siwavutike mundhu yujha wamng'anamuka Mwana wa Mundhu! Idakakhala mbasa kwa mundhu mmeneyo kuti siwadakabadwa.”
25Ndiipo Yuda, yujha wamng'anamuka, wadakamba, “Oyaluza, nde ine kani?”
Yesu wadamuyangha, “Yetu, nde iwe ngati umo wakambila.”
Chakudya cha Ambuye
Maluko 14:22-26; Luka 22:14-20; 1 Akolinso 11:23-25
26Yapo amadya Yesu wadatenga bumunda, wadayamika, wadaubandhula, ni kwapacha oyaluzidwa wake nikukamba, “Tengani mudye, ili nithupi langa.”
27Ndiipo wadatenga chikho, wadayamika Mnungu, ni kwaapacha oyaluzidwa wake niwakamba, “Mwaonjhe mchimwele chikho ichi, 28uwu nde mwazi wanga uwo uchimikiza chipangano, umwazika ndande ya ambili dala machimo yao yalekeleledwe. 29Nikukambilani, sinimwanjho divai iyi mbaka siku ilo sinimwe divai yachipano ni anyiimwe mu Ufumu wa Atate wanga.”
30Ndiipo adaimba nyimbo nikupita kuphili la Mizeituni.
Yesu walosa kuti Petulo siwamkane
Maluko 14:27-31; Luka 22:31-34; Yohana 13:36-38
31Ndiipo Yesu wadaakambila, “Usiku uno walelo anyiimwe mwaonjhe simunithawe ni kunisiya, pakuti malembo yakamba, ‘Sinimbule owesa, ni mbele sizimwazike.’ 32Nambho yapo sinihyuke, sinikuchogoleleni kupita ku jhiko la Galilaya.”
33Petulo wadamuyangha, “Ata ngati onjhe siakusiye, ine sinikusiya.”
34Yesu wadamkambila Petulo, “Zene nikukambila, usiku wa lelo, wakali osalile tambala, siunikane katatu.”
35Petulo wadayangha, “Sinikhoza kukukana, ata ngati nikafunika kumwalila pamojhi ni namwe sinikukanani!”
Ni oyaluzidwa wonjhe adakamba chimwecho.
Yesu wapembhela ku busitani ya Getisemane
Maluko 14:32-42; Luka 22:39-46
36Ndiipo Yesu wadapita pamojhi ni oyaluzidwa wake pa malo yapo pamatanidwa Getisemani, ni iye wadaakambila, “Khalani pano ine nipite yapo kukapembhela.”
37Wadatenga Petulo ni wana awili Azebedayo, wadayamba kuva chizoni ni kulaga mumtima. 38Kumeneko wadaakambila, “Nili ni chisoni chachikulu mumtima mwanga icho chikhoza kunipha. Khalani pano ni muchezele pamojhi ni ine.”
39Wadapita pachogolo pang'ono, wadagwa panjhi chifufumimba ni kupembhela, “Atate wanga, ngati ikhozeka, nichocheleni chikho ichi cha mavuto! Chipano osati ngati umo nifunila ine, nambho ngati umo mufunila imwe.”
40Ndiipo wadabwela kwa oyaluzidwa wake ni kwaapheza agona, wadamkambila Petulo, “Ikhala bwanji simdakhoze kuchezelela ni ine ata kwa saa imojhipe? 41Chezelani ni kupembhela kuti msadalowa mu mayeselo. Mtima ufuna kuchita yayo yafunika, nambho thupi lilibe mbhavu.”
42Wadapitanjho kakawili wadapembhela, “Atate wanga, ngati siikhozeka kuchichocha chikho ichi chamavuto, basi mchite umo mfunila.” 43Yapo wadabwela kakawili wadaaphezanjho agonanjho ndande maso yao yadali ni litulo.
44Chimwecho wadaasiyanjho ni kupita kupembhela kakatatu ni wakamba mau yamweyajha. 45Ndiipo wadabwela kwa oyaluzidwa wake ni kwakambila, “Bwanji, mkali kugona ni kupumulila? Vechelani, saa yakwana Mwana wa Mundhu siwagwilidwe ni wandhu amachimo. 46Imani tijhipita. Yujha waning'anamuka watokujha.”
Yesu wagwilidwa
Maluko 14:43-50; Luka 22:47-53; Yohana 18:3-12
47Yesu yapo wadali wakali kuyendekela kukamba, Yuda mmojhi wa oyaluzidwa wake khumi ni awili, wadajha. Yuda wadachogozana ni gulu lalikulu la wandhu yawo adali ni maupanga ni vibonga, yawo adatumidwa ni waakulu akulu anjhukulu ni wakulu a wandhu. 48Yuda wadapacha wandhu wajha chizindikilo kuti, “Mundhu uyo sinimlonjhele kwa kumvumbatila nde mmweyo, mgwileni!”
49Pamenepo Yuda wadajha kwa Yesu ni kumlonjela, “Moni oyaluza,” pampajha wadamvumbatila.
50Yesu wadamkambila, “Iwe bwenji, chita chijha wajha kuchichita.”
Ndiipo wandhu wajha adamsendelela Yesu adamgwila ni kummanga.
51Mmojhi wa wajha adali ni Yesu wadasolomola upanga ni kudula khutu la mbowa wa mjhukulu Wamkulu. 52Ndiipo Yesu wadamkambila, “Bwezela upanga wako mmalo mwake, pakuti waliyonjhe wakupha kwa upanga, siwaphedwe kwa upanga. 53Bwanji, simjhiwa kuti nikhoza kwatana Atate wanga anithangatile, ni iwo akhoza kunipelekela magulu khumi ni yawili ya atumiki akumwamba? 54Nambho, malembo yoyela siyakwanile bwanji yajha yakamba kuti, nde umo ifunikila ichitike?”
55Ndiipo Yesu wadalikambila lijha gulu, “Bwanji, mwajha ni maupanga ni vibonga kunigwila ine ngati wolanda? Kila siku nidali namwe ni niyaluza mnyumba ya Mnungu, simudanigwile. 56Ivi vonjhe vachokela kuti vijha valembedwa ni alosi vikwanile.”
Ndiipo oyaluzidwa wake wonjhe adamsiya ni kumthawa.
Yesu pachogolo pa bwalo
Maluko 14:53-65; Luka 22:54-55,63-71; Yohana 18:13-14,19-24
57Wajha adamgwila Yesu adampeleka ku nyumba ya mjhukulu wamkulu uyo wamatanidwa Kayafa, pa malo yapo adasonghana oyaluza a thauko pamojhi ni wakulu a wandhu. 58Petulo wadachata Yesu kwa patali mbaka kwa mjhukulu wamkulu. Wadalowa mkati mwa seli pamojhi ni alonda kuti waone icho sichichokele.
59Ajhukulu wa wakulu ni bwalo lonjhe, adafunafuna umboni wamthila dala amphe Yesu. 60Nambho sadakhoze kupata umboni walionjhe, ata ngati wandhu adachocha umboni wambili wamthila. Ndiipo adajha amboni awili, 61adakamba, “Mundhu uyu wadakamba, ‘Sinikhoze kuibomola Nyumba ya Mnungu ni kuimanganjho pa masiku yatatu.’ ”
62Ndiipo Mkulu wa ajhukulu wadaima ni kumkambila Yesu, “Bwanji, siuyangha chalichonjhe? Bwanji milandu iyo akamba wandhu anyiyawa ya uzene?” 63Nambho Yesu wadakhala chete. Mkulu wa Ajhukulu wadakamba, “Chipano lumbila mjhina la Mnungu wali wamoyo, utikambile ngati iwe nde Kilisito, Mwana wa Mnungu.”
64Yesu wadamuyangha, “Umo ukambila nde chimwecho! Nambho nikukambilani mwaonjhe, kuyambila chipano simumuone Mwana wa Mundhu wakhala kwene kwa Mnungu Wambhavu, niwajha mmitambo!” 65Pampajha Mkulu wa ajhukulu wadang'amba njhalu zake kulangiza kuti wakwiya, ni kukamba, “Wakafula! Tifunanjho umboni unjake? Mwachinawene mwavela umo wakhafulila. 66Anyiimwe muganiza chiyani?”
Anyiiwo adayangha, “Walakwa uyu ni wafunika waphedwe.”
67Ndiipo adamlavulila malovu kumaso ni kumbula. Wina adammenya makofi, 68adakamba, “Iwe Kilisito, tilosele! Yani uyo wakubula?”
Petulo wamkana Yesu
Maluko 14:66-72; Luka 22:56-62; Yohana 18:15-18,25-27
69Petulo wadakhala kubwalo kuseli. Mbowa mmojhi wamkazi wadampitila ni kumkambila, “Iwe nawenjho udali pamojhi ni Yesu wa ku Galilaya.”
70Petulo wadakana pamaso pawo onjhe, niwakamba, “Sinichijhiwa icho uchikamba.” 71Yapo wadatuluka kubwalo ni kufika pakhomo, mbowa mwina wamkazi wadamuona, wadaakambila wandhu yawo adali pamenepo, “Mundhu uyu wadali pamojhi ni Yesu wa ku Nazaleti.”
72Petulo wadakangalanjho kwa kulumbila uku ni wakamba, “Sinimjhiwa mundhu mmeneyo!”
73Pambuyo pang'ono, anyiwajha adali pajha adampitila Petulo wadamkambila, “Zenedi, iwe ni mmojhi wao, pakuti ata kukamba kwako kulangiza kuti iwe uchoka ku Galilaya!”
74Ndiipo Petulo wadayamba kujhileswa ni kulumbila, “Zenedi sinimjhiwa mundhu uyu!”
Pampajha tambala wadalila. 75Ndiipo Petulo wadakumbukila mau yajha wadakamba Yesu, “Tambala wakali osalile, siunikane katatu.” Wadapita kubwalo, wadalila kwa kubuula.

Currently Selected:

Matayo 26: NTNYBL2025

Highlight

Share

Copy

None

Want to have your highlights saved across all your devices? Sign up or sign in