1
Yohana 5:24
Nyanja
NTNYBL2025
“Zene nikukambilani, mundhu waliyonjhe uyo wavela mawu yanga ni kwaakhulupilila Amnungu yawo anituma, ali ni umoyo wa muyaya. Sialamulidwa muyaya, nambho wachoka kunyifa ni kulowa kuumoyo.
Compare
Explore Yohana 5:24
2
Yohana 5:6
Yesu yapo wadamuona mundhu mmeneyo wagona pamenepo ni kujhiwa kuti wadakhala kwa ndhawi ya itali, wadamfunjha, “Bwanji, ufuna kulama?”
Explore Yohana 5:6
3
Yohana 5:39-40
Anyiimwe muyapenyechecha Malembo Yoyela kwa kuganizila kuti simpate umoyo wa muyaya kwa kuyapenyechecha, nambho malembo yaya yanichochela umboni ine! Chimwecho simufuna kujha kwanga kuti mpate umoyo.”
Explore Yohana 5:39-40
4
Yohana 5:8-9
Yesu wadamkambila, “Ima tenga chika lako ujhiyenda.” Pampajha mundhu mmeneyo wadalama, wadatenga chika lake ni kuyamba kuyenda. Chindhu ichi chidachitika Siku lo Pumulila.
Explore Yohana 5:8-9
5
Yohana 5:19
Yesu wadakambila, “Uzene nikukambilani, Mwana siwakhoza kuchita chindhu yokha, icho wachiona Atate wake achita, nde icho Mwana wakhoza kuchichita.
Explore Yohana 5:19
Home
Bible
Plans
Videos