1
Lk. 2:11
Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa
BLY-DC
Usiku womwe uno m'mudzi wa Davide wakubadwirani Mpulumutsi, amene ndi Khristu Ambuye.
Compare
Explore Lk. 2:11
2
Lk. 2:10
Koma mngeloyo adaŵauza kuti, “Musaope, ndadzakuuzani uthenga wabwino, umene udzakondweretsa anthu onse kwambiri.
Explore Lk. 2:10
3
Lk. 2:14
“Ulemerero kwa Mulungu Kumwambamwamba, ndipo pansi pano mtendere pakati pa anthu amene Iye amakondwera nawo.”
Explore Lk. 2:14
4
Lk. 2:52
Ndipo Yesu analikunka nakula m'nzeru ndi mu msinkhu, ndipo Mulungu ndi anthu omwe ankakondwera naye kwambiri.
Explore Lk. 2:52
5
Lk. 2:12
Chitsimikizo chake ndi ichi: mukapeza mwana wakhanda, wokutidwa ndi nsalu, atagona m'chodyera cha zoŵeta.”
Explore Lk. 2:12
6
Lk. 2:8-9
Ku dera lomwelo kunali abusa amene ankalonda zoŵeta zao ku dambo usiku. Mwadzidzidzi mngelo wa Ambuye adadzaimirira pakati pao, ndipo ulemerero wa Ambuye udaŵala ponse pozungulira, mwakuti abusawo adaachita mantha kwambiri.
Explore Lk. 2:8-9