1
AFILIPI 3:13-14
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
BLPB2014
Abale, ine sindiwerengera ndekha kuti ndatha kuchigwira: koma chinthu chimodzi ndichichita; poiwaladi zam'mbuyo, ndi kutambalitsira zam'tsogolo, ndilondetsa polekezerapo, kutsatira mfupo wa maitanidwe akumwamba a Mulungu a mwa Khristu Yesu.
Compare
Explore AFILIPI 3:13-14
2
AFILIPI 3:10-11
kuti ndimzindikire Iye, ndi mphamvu ya kuuka kwake, ndi chiyanjano cha zowawa zake, pofanizidwa ndi imfa yake; ngati nkotheka ndikafikire kuuka kwa akufa.
Explore AFILIPI 3:10-11
3
AFILIPI 3:8
Komatu zenizeninso ndiyesa zonse zikhale chitayiko chifukwa cha mapambanidwe a chizindikiritso cha Khristu Yesu Ambuye wanga, chifukwa cha Iyeyu ndinatayikitsa zinthu zonse, ndipo ndiziyesa zapadzala, kuti ndikadzionjezere Khristu
Explore AFILIPI 3:8
4
AFILIPI 3:7
Komatu zonse zimene zinandipindulira, zomwezo ndinaziyesa chitayiko chifukwa cha Khristu.
Explore AFILIPI 3:7
Home
Bible
Plans
Videos