1
ESTERE 8:17
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
BLPB2014
Ndi m'maiko monse, ndi m'midzi yonse, mudafika mau a mfumu ndi lamulo lake, Ayuda anali nako kukondwera ndi chimwemwe, madyerero ndi tsiku lokoma. Ndipo ambiri a mitundu ya anthu a m'dziko anasanduka Ayuda; pakuti kuopsa kwa Ayuda kudawagwera.
Compare
Explore ESTERE 8:17
2
ESTERE 8:11
m'menemo mfumu inalola Ayuda okhala m'midzi iliyonse asonkhane, ndi kulimbikira moyo wao, kuononga, kupha, ndi kupulula mphamvu yonse ya anthu ndi ya dziko yofuna kuwathira nkhondo, iwo, ana ang'ono ao, ndi akazi ao, ndi kulanda zofunkha zao
Explore ESTERE 8:11