1
ESTERE 7:3
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
BLPB2014
Nayankha mkazi wamkulu Estere, nati, Ngati mwandikomera mtima, mfumu, ndipo chikakomera mfumu, andilekere moyo wanga pa kupempha kwanga, ndi wa anthu a mtundu wanga pa pempho langa
Compare
Explore ESTERE 7:3
2
ESTERE 7:10
Nampachika Hamani pa mtengo adaukonzera Mordekai. Pamenepo mkwiyo wa mfumu unatsika.
Explore ESTERE 7:10