1
1 AKORINTO 5:11
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
BLPB2014
koma tsopano ndalembera inu kuti musayanjane naye, ngati wina wotchedwa mbale ali wachigololo, kapena wosirira, kapena wopembedza mafano, kapena wolalatira, kapena woledzera, kapena wolanda, kungakhale kukadya naye wotere, iai.
Compare
Explore 1 AKORINTO 5:11
2
1 AKORINTO 5:7
Tsukani chotupitsa chakale, kuti mukakhale mtanda watsopano, monga muli osatupa. Pakutinso Paska wathu waphedwa, ndiye Khristu
Explore 1 AKORINTO 5:7
3
1 AKORINTO 5:12-13
Pakuti nditani nao akunja kukaweruza iwo? Kodi amene ali m'katimo simuwaweruza ndi inu, koma akunja awaweruza Mulungu? Chotsani woipayo pakati pa inu nokha.
Explore 1 AKORINTO 5:12-13
Home
Bible
Plans
Videos