1
Miyambo 21:21
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
CCL
Amene amatsata chilungamo ndi kukhulupirika, amapeza moyo ndi ulemerero.
Compare
Explore Miyambo 21:21
2
Miyambo 21:5
Zolinga za munthu wakhama zimachulukitsa zinthu zake; koma aliyense wochita zinthu mofulumira amadzakhala wosauka.
Explore Miyambo 21:5
3
Miyambo 21:23
Amene amagwira pakamwa pake ndi lilime lake sapeza mavuto.
Explore Miyambo 21:23
4
Miyambo 21:2
Makhalidwe a munthu amaoneka olungama kwa mwini wakeyo, koma Yehova ndiye amayesa mtima wake.
Explore Miyambo 21:2
5
Miyambo 21:31
Kavalo amamukonzera tsiku la nkhondo, koma ndi Yehova amene amapambanitsa.
Explore Miyambo 21:31
6
Miyambo 21:3
Za chilungamo ndi zolondola ndi zomwe zimakondweretsa Yehova kuposa kupereka nsembe.
Explore Miyambo 21:3
7
Miyambo 21:30
Palibe nzeru, palibe kumvetsa bwino, palibenso uphungu, zimene zingapambane Yehova.
Explore Miyambo 21:30
8
Miyambo 21:13
Amene atsekera mʼkhutu mwake wosauka akamalira, nayenso adzalira koma palibe adzamuyankhe.
Explore Miyambo 21:13