1
Ezekieli 15:8
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
CCL
Ine ndidzasandutsa dziko kukhala chipululu chifukwa anthu akhala osakhulupirika, akutero Ambuye Yehova.’ ”
Compare
Explore Ezekieli 15:8
2
Ezekieli 15:7
Ndidzawalanga pamenepo ngakhale iwo atuluka pa moto, motowo udzawatenthabe. Ndipo pamene ndidzatsutsana nawo, mudzadziwa kuti Ine ndine Yehova.
Explore Ezekieli 15:7